2 Mafumu 8

Wa ku Sunemu abwera kwao itatha njalayo 1 Ndipo Elisa ananena ndi mkazi uja adamuukitsira mwana wace, kuti, Nyamuka, numuke iwe ndi banja lako, nugonere komwe ukaone malo; pakuti Yehova…

2 Mafumu 9

Yehu adzozedwa mfumu ya Israyeli 1 Ndipo Elisa mneneriyo anaitana mmodzi wa ana a aneneri, nanena naye, Udzimangire m’cuuno, nutenge nsupa iyi ya mafuta m’dzanja mwako, numuke ku Ramoti Gileadi….

2 Mafumu 10

Yehu aononga mbumba ya Ahabu 1 Ndipo Ahabu anali nao ana amuna makumi asanu ndi awiri m’Samariya. Nalemba akalata Yehu, natumiza ku Samariya kwa akulu a Yezreeli, ndiwo akulu akulu,…

2 Mafumu 11

A taliya aononga mbumba yacifumu ya Yuda; apulumuka Yoasi, aphedwa Ataliya 1 Pamene Ataliya mace wa Ahaziya anaona kuti mwana wace wafa, ananyamuka, naononga mbeu yonse yacifumu. 2 Koma Yoseba…

2 Mafumu 12

Yoasi akonza Kacisi 1 Caka cacisanu ndi ciwiri ca Yehu, Yoasi analowa ufumu wace; nakhala mfumu m’Yerusalemu zaka makumi anai; ndi dzina la mai wace ndiye Zibiya wa ku Beereseba….

2 Mafumu 13

Yoahazi mfumu ya Israyeli 1 Caka ca makumi awiri ndi zitatu ca Yoasi mwana wa Ahaziya mfumu ya Yuda, Yoahazimwana wa Yehu analowa ufumu wace wa Israyeli ku Samariya, nakhala…

2 Mafumu 14

Amaziyamfumu ya Yuda, Yoasi ndi Yerobiamu waciwiri mafumu a Israyeli 1 Caka caciwiri ca Yoasi mwana wa Yoahazi mfumu ya Israyeli, Amaziya mwana wa Yoasi mfumu ya Yuda analowa ufumu…

2 Mafumu 15

Azariya mfumu ya Yuda 1 Caka ca makumi awiri mphambu zisanu ndi ziwiri ca Yerobiamu mfumu ya Israyeli, Azariya mwana wa Amaziya mfumu ya Yuda analowa ufumu wace. 2 Anali…

2 Mafumu 16

Ahazi mfumu ya Yuda 1 Caka cakhumi mphambu zisanu ndi ziwiri ca Peka mwana wa Remaliya Ahazi mwana wa Yotamu mfumu ya Yuda analowa ufumu wace. 2 Ahazi anali wa…

2 Mafumu 17

Hoseyamfumu yotsiriza ya Israyeli, Salimanezeri mfumu ya Asuri apasula Samariya, Aisrayeli natengedwa ukapolo 1 Caka cakhumi ndi ziwiri ca Ahazi mfumu ya Yuda Hoseya mwana wa Ela analowa ufumu wace…