1 Mafumu 20
Nkhondo pakati pa Ahabu ndi Benihadadi 1 Ndipo Benihadadi mfumu ya Aramu anamemeza khamu lace lonse la nkhondo; ndi mafumu makumi atatu mphambu awiri anali naye, pamodzi ndi akavalo ndi…
Nkhondo pakati pa Ahabu ndi Benihadadi 1 Ndipo Benihadadi mfumu ya Aramu anamemeza khamu lace lonse la nkhondo; ndi mafumu makumi atatu mphambu awiri anali naye, pamodzi ndi akavalo ndi…
Yezebeli aphetsa Naboti 1 Ndipo zitatha izi, kunaoneka zotere: Naboti wa ku Yezreeli anali ndi munda wamphesa, unali m’Yezreelimo, m’mbali mwa nyumba ya Ahabu mfumu ya ku Samaria. 2 Ndipo…
Ahabu apangana ndi Yehosafati 1 Ndipo Aaramu ndi Aisrayeli anakhala cete zaka zitatu, osathirana nkhondo. 2 Koma kunacitika caka cacitatu, kuti Yehosafati mfumu ya Yuda anatsikira kwa mfumu ya Israyeli….
Eliya ndi nthenda ya Ahaziya 1 NDIPO atamwalira Ahabu, Moabu anapandukana ndi Israyeli. 2 Ndipo Ahaziya anagwa kubzola ku made wa cipinda cace cosanja cinali ku Samariya, nadwala, natuma mithenga,…
Eliya atengedwa kunka Kumwamba 1 Ndipo kunali, pamene Yehova adati akweze Eliya kumwamba ndi kabvumvulu, Eliya anacokera ku Giligala pamodzi ndi Elisa. 2 Ndipo Eliya anati kwa Elisa, Ukhale pompano…
Cipulumutso codabwitsa ca nkhondo za Yuda, Israyeli, ndi Edomu 1 Ndipo Yehoramu mwana wa Ahabu analowa ufumu wa Israyeli m’Samariya m’caka cakhumi mphambu zisanu ndi zitatu ca Yehosafati mfumu ya…
Elisa afurukitsa mafuta a mkazi wamasiye 1 Ndipo wina wa akazi a ana a aneneri anapfuula kwa Elisa, ndi kuti, Mnyamata wanu, mwamuna wanga wafa; mudziwa kuti mnyamata wanu anaopa…
Namani wakhateyo aciritsidwa 1 Ndipo Namani kazembe wa khamu la nkhondo la mfumu ya Aramu anali munthu womveka pamaso pa mbuyace, ndi waulemu; popeza mwa iye Yehova adapulumutsa Aaramu; ndiyenso…
Elisa ayandamitsa citsulo pamadzi 1 Ndipo ana a aneneri anati kwa Elisa, Taonani tsono, pamalo tikhalapo ife pamaso panu paticepera 2 Mutilole tipite ku Yordano, tikatengeko, ali yense mtengo, tidzimangire…
1 Ndipo Elisa anati, Mverani mau; a Yehova; atero Yehova, Mawa dzuwa lino adzagula muyeso wa ufa ndi sekeli, adzagulanso miyeso iwiri ya barele ndi sekeli, pa cipata ca Samariya….