1 Mafumu 10
Mfumu yaikazi ya ku Seba adzaceza kwa Solomo ku Yerusalemu 1 Ndipo atamva mfumu yaikazi ya ku Seba mbiri ya Solomo yakubukitsa dzina la Yehova, anadza kumuyesera iye ndi miyambi…
Mfumu yaikazi ya ku Seba adzaceza kwa Solomo ku Yerusalemu 1 Ndipo atamva mfumu yaikazi ya ku Seba mbiri ya Solomo yakubukitsa dzina la Yehova, anadza kumuyesera iye ndi miyambi…
Solomo adzipereka kupembedza mafano; Mulungu aipidwa naye 1 Ndipo mfumu Solomo anakonda akazi ambiri acilendo, pamodzi ndi mwana wamkazi wa Farao, akazi a ku Moabu, ndi a ku Amoni, ndi…
Rehabiamu sam vera uphungu wa akuru 1 Ndipo Rehabiamu anamka ku Sekemu, popeza Aisrayeli onse anadza ku Sekemu kumlonga ufumu. 2 Ndipo kunali kuti Yerobiamu mwana wa Nebati anacimva akali…
Mneneri adzudzula Yerobiamu 1 Ndipo onani, munthu wa Mulungu anacokera ku Yuda mwa mau a Yehova nadza ku Beteli; ndipo Yerobiamu anali kuimirira m’mbali mwa guwa la nsembe kufukiza zonunkhira….
Ahiya aneneratu kugwa kwa Yerobiamu 1 Nthawi yomweyo Abiya mwana wa Yerobiamu anadwala. 2 Ndipo Yerobiamu ananena ndi mkazi wace, Unyamuke, nudzizimbaitse, ungadziwike kuti ndiwe mkazi wa Yerobiamu, nupite ku…
Abiya atsata zoipa za atate wace Rehabiamu 1 Ndipo caka cakhumi mphambu zisanu ndi zitatu ca mfumu Yerobiamu mwana wa Nebati, Abiya analowa ufumu wa Yuda. 2 Anakhala mfumu zaka…
Yehu aneneratu kugwa kwa Basa 1 Ndipo mau a Yehova akutsutsa Basa anadza kwa Yehu mwana wa Hanani, nati, 2 Popeza ndinakukuza iwe kucokera kupfumbi, ndi kukuika iwe mfumu ya…
Mneneri Eliya ku Keriti 1 Ndipo Eliya wa ku Tisibe wokhala ku Gileadi ananena ndi Ahabu, nati, Pali Yehova Mulungu wa Israyeli, amene ndimakhala pamaso pace, ngati adzagwa mame kapena…
Eliya ndi Abaala ku Karimeli 1 Ndipo atapita masiku ambiri, mau a Yehova anafika kwa Eliya caka cacitatu, nati, Kadzionetse kwa Ahabu, ndipo ndidzatumiza mvula padziko. 2 Ndipo Eliya anamka…
Eliya athawa Yezebeli 1 Ndipo Ahabu anauza Yezebeli zonse anazicita Eliya, ndi m’mene anawaphera ndi lupanga aneneri onsewo, 2 Tsono Yezebeli anatuma mthenga kwa Eliya, wakuti, Milungu indilange nionjezepo, ngati…