Genesis 21

Kubadwa kwa Isake 1 Ndipo Yehova anayang’anira Sara monga momwe anati, ndipo Yehova anamcitira iye monga ananena. 2 Ndipo Sara anatenga pakati, nambalira Abrahamu m’ukalamba wace mwana wamwamuna, nthawi yomweyo…

Genesis 22

Isake aperekedwa nsembe 1 Ndipo panali zitapita zimenezo, Mulungu anamuyesa Abrahamu nati kwa iye, Abrahamu; ndipo anati, Ndine pano. 2 Ndipo anati, Tengatu mwana wako, wamwamuna wayekhayo, Isake, amene ukondana…

Genesis 23

Imfa ndi kuikidwa kwa Sara 1 Ndipo Sara anali wa zaka zana limodzi kudza makumi awiri ndi zisanu ndi ziwiri: ndizo zaka za moyo wa Sara. 2 Ndipo Sara anafa…

Genesis 24

Rebeka apalidwa ubwenzi ndi Isake 1 Ndipo Abrahamu anali wokalamba, nagonera zaka zambiri; ndipo Yehova anadalitsa Abrahamu m’zinthu zonse. 2 Ndipo Abrahamu anati kwa mnyamata wace wamkuru wa pa nyumba…

Genesis 25

Kumwalira kwa Abrahamu 1 Ndipo Abrahamu anatenga mkazi wina dzina lace Ketura. 2 Ndipo anambalira iye Zimerani ndi Yokesani ndi Medani, ndi Midyani, ndi Yisebaki, ndi Sua. 3 Ndipo Yokesani…

Genesis 26

Isake akhala kwa Afilisti 1 Ndipo panali njala padzikopo, yoyenjezeka ndi njala yoyamba ija imene inali masiku a Abrahamu, ndipo Isake ananka kwa Abimeleke mfumu ya Afilisti ku Gerari. 2…

Genesis 27

Yakobo adalitsidwa m’malo mwa Esau 1 Ndipo panali atakalamba Isake, ndi maso ace anali a khungu losaona nalo, anamuitana Esau mwana wace wamwamuna wamkuru, nati kwa iye, Mwana wanga; ndipo…

Genesis 28

1 Ndipo Isake anamuitana Yakobo, namdalitsa iye, namuuza iye, nati kwa iye, Usatenge mkazi wa ana akazi a Kanani. 2 Tauka, nupite ku Padanaramu, ku nyumba ya Betuele, atate wa…

Genesis 29

Yakobo akomana ndi Rakele 1 Ndipo Yakobo ananka ulendo wace, nafika ku dziko la anthu a kum’mawa. 2 Ndipo anayang’ana, taonani, citsime m’dambo, ndipo, taonani, magulu atatu a nkhosa alinkugona…

Genesis 30

1 Pamene Rakele anaona kuti sanambalira Yakobo ana, Rakele anamcitira mkuru wace nsanje; nati kwa Yakobo, Ndipatse ana ndingafe. 2 Ndipo Yakobo anapsa mtima ndi Rakele; nati, Kodi ine ndikhala…