2 Samueli 4

Isiboseti aphedwa, Davide alanga omupha 1 Ndipo pamene Isiboseti mwana wa Sauli, anamva kuti Abineri adakafera ku Hebroni, manja ace anafoka, ndi Aisrayeli onse anabvutika. 2 Ndipo Isiboseti, mwana wa…

2 Samueli 5

Mafuko onse abvomereza Davide mfumu yao 1 Pomwepo mafuko onse a Israyeli anabwera kwa Davide ku Hebroni, nalankhula nati, Taonani, ife ndife pfupa lanu ndi mnofu wanu. 2 Masiku anapitawo,…

2 Samueli 6

Atenga likasa la Mulungu ku nyumba ya Abinadabu 1 Pambuyo pace Davide anamemezanso osankhika onse a m’Israyeli, anthu zikwi makumiatatu. 2 Ndipo Davide ananyamuka, namuka nao anthu onse anali naye,…

2 Samueli 7

Mulungu salola Davide ammangire nyumba 1 Ndipo kunali pakukhala mfumuyo m’nyumba mwace, atampumulitsa Yehova pa adani ace onse omzungulira, 2 mfumuyo inanena ndi Natani mneneriyo, Onani ndirikukhala ine m’nyumba yamikungudza,…

2 Samueli 8

Davide agonjetsa amitundu ena 1 Ndipo m’tsogolo mwace Davide anakantha Afilisti, nawagonjetsa; Davide nalanda mudzi wa Metege Ama m’manja mwa Afilisti. 2 Ndipo anakantha Amoabu nawayesa ndi cingwe, nawagonetsa pansi;…

2 Samueli 9

Davide acitira Mefiboseti mwana wa Jonatani cifundo 1 Ndipo Davide anati, Kodi atsalako wina wa nyumba ya Sauli, kuti ndimcitire cifundo cifukwa ca Jonatani? 2 Ndipo panali mnyamata wa m’nyumba…

2 Samueli 10

Davide akantha Aamoni ndi Aaramu 1 Ndipo kunali zitapita izi, mfumu ya ana a Amoni inamwalira, ndipo Hanuni mwana wace anakhala mfumu m’malo mwace. 2 Ndipo Davide anati, Ndidzacitira Hanuni…

2 Samueli 11

Chimo loopsa la Davide 1 Ndipo kunali pofikanso caka, nyengo yakuturuka mafumu, Davide anatumiza Yoabu, pamodzi ndi anyamata ace, ndi Aisrayeli onse; ndipo iwo anasakaza ana a Amoni, naumangira misasa…

2 Samueli 12

Kulapa ndi kulangidwa kwa Davide 1 Ndipo Yehova anatumiza Natani kwa Davide. Ndipo anafika kwa iye nanena naye, Pa mudzi wina panali anthu awiri; wina wolemera, wina wosauka. 2 Wolemerayo…

2 Samueli 13

Chimo loopsa la Amnoni 1 Ndipo kunali citapita ici, popeza Abisalomu mwana wa Davide anali naye mlongo wace wokongola, dzina lace ndiye Tamara, Amnoni mwana wa Davide anamkonda iye. 2…