1 Samueli 25

Amwalira Samueli 1 Ndipo Samueli anamwalira; ndi Aisrayeli onse anaunjikana pamodzi nalira maliro ace, namuika m’nyumba yace ku Rama. Davide nanyamuka, natsikira ku cipululu ca Parana. Za Davide, Nabala ndi…

1 Samueli 26

Davide alekanso Sauli osamupha 1 Ndipo Azifi anafika kwa Sauli ku Gibeya, nati, Kodi Davide sali kubisala m’phiri la Hagila, kupenya kucipululu! 2 Ndipo Sauli ananyamuka, natsikira ku cipululu ca…

1 Samueli 27

1 Ndipo Davide ananena mumtima mwace, Tsiku tina Sauli adzandipha; palibe cina condikomera koma kuti ndithawire ku dziko la Afilisti; ndipo Sauli adzakhala kakasi cifukwa ca ine, osandifunanso m’malire onse…

1 Samueli 28

Sauli afunsira mkazi wobwebweta ku Endori 1 Ndipo kunali masiku aja, Afilisti anasonkhanitsa pamodzi makamu ao onse kunkhondo, kuti akaponyane ndi Aisrayeli. Ndipo Akisi ananena ndi Davide, Dziwa kuti zoonadi,…

1 Samueli 29

Afilisti abweza Davide kunkhondo 1 Tsono Afilisti anasonkhanitsa makamu ao onse ku Afeki; ndipo Aisrayeli anamanga ku citsime ca m’Jezreeli. 2 Ndipo akalonga a Afilisti ananyamuka ndi mazana ao ndi…

1 Samueli 30

Davide alanditsa a ku Zikilaga m’manja mwa Aamaleki 1 Ndipo kunali, pakufika Davide ndi anthu ace ku Zikilaga tsiku lacitatu, Aamaleki adaponya nkhondo yobvumbulukira kumwera, ndi ku Zikilaga, nathyola Zikilaga…

1 Samueli 31

Sauli ndi ana ace atatu aphedwa ndi Afilisti pa Giliboa 1 Ndipo Afilisti anaponyana ndi Aisrayeli; Aisrayeli nathawa pamaso pa Afilisti, nagwa olasidwa m’phiri la Giliboa. 2 Ndipo Afilisti anapitikitsa,…

2 Samueli 1

Amuuza Davide za imfa ya Sauli 1 NDIPO kunali atamwalira Sauli, pamene Davide anabwera atawapha Aamaleki, ndipo Davide atakhala ku Zikilaga masiku awiri; 2 pa tsiku lacitatu, onani, munthu anaturuka…

2 Samueli 2

Davide alowa ufumu wa Yuda 1 Ndipo zitatha izi Davide anafunsira kwa Yehova nati, Kodi ndikwere kunka m’mudzi wina wa Yuda? Ndipo Yehova ananena naye, Kwera. Davide nanena naye, Ndikwere…

2 Samueli 3

1 Ndipo panali nkhondo nthawi yaitali pakati pa nyumba ya Sauli ndi nyumba ya Davide. Koma Davide analimba cilimbire, ndi nyumba ya Sauli inafoka cifokere. Ana obadwira Davide ku Hebroni…