1 Samueli 15
Sauli alamulidwa aononge Amaleki 1 Ndipo Samueli ananena ndi Sauli, Yehova ananditumiza ine kukudzozani mukhale mfumu ya anthu ace Aisrayeli; cifukwa cace tsono mumvere kunena kwa mau a Yehova. 2…
Sauli alamulidwa aononge Amaleki 1 Ndipo Samueli ananena ndi Sauli, Yehova ananditumiza ine kukudzozani mukhale mfumu ya anthu ace Aisrayeli; cifukwa cace tsono mumvere kunena kwa mau a Yehova. 2…
Samueli adzoza Davide akhale mfumu 1 Ndipo Yehova ananena ndi Samueli, Iwe ukuti ulire cifukwa ca Sauli nthawi yotani, popeza Ine ndinamkana kuti asakhale mfumu ya Israyeli? Dzaza nyanga yako…
Davide apha Goliati 1 Pamenepo Afilisti anasonkhanitsa makamu ao a nkhondo, naunjikana ku Soko wa ku Yuda, namanga zithando pakati pa Soko ndi Azeka ku Efesi-damimu. 2 Ndipo Sauli ndi…
Ubwenzi wa Davide ndi Jonatani 1 Ndipo kunali, pakutsiriza iye kulankhula ndi Sauli, mtima wa Jonatani unalumikizika ndi mtima wa Davide, ndipo Jonatani anamkonda iye monga moyo wa iye yekha….
Jonatani anenera Davide kwa Sauli 1 Ndipo Sauli analankhula kwa Jonatani mwana wace, ndi anyamata ace onse kuti amuphe Davide. 2 Koma Jonatani mwana wa Sauli anakondwera kwambiri ndi Davide….
Pangano pakati pa Davide ndi Jonatani 1 Ndipo Davide anathawa ku Nayoti m’Rama, nadzanena pamaso pa Jonatani, Ndacitanji ine? kuipa kwanga kuli kotani? ndi chimo langa la pamaso pa atate…
Davide athawira kwa wansembe Ahimeleki ku Nobi 1 Ndipo Davide anafika ku Nobi kwa! Ahimeleki wansembeyo; ndipo Ahimeleki anadza kukomana ndi Davide alikunjenjemera, nanena naye, Muli nokha bwanji, palibe munthu…
Davide apulumukira ku phanga La Adulamu 1 Motero Davide anacoka kumeneko, napulumukira ku phanga la ku Adulamu; ndipo pamene abale ace ndi banja lonse la atate wace anamva, iwo anatsikira…
Davide alanditsa a ku Keila 1 Tsono anauza Davide, kuti, Onani Afilisti alikuponyana ndi Keila, nafunkha za m’madwale. 2 Cifukwa cace Davide anafunsira kwa Yehova, nati, Ndimuke kodi kukakantha Afilisti…
Davide aleka Sauli osamupha 1 Ndipo kunali, pakubwerera Sauli potsata Afilisti, anamuuza, kuti, Taonani, Davide ali ku cipululu ca Engedi. 2 Tsono Sauli anatenga anthu zikwi zitatu osankhika pakati pa…