Oweruza 20

Aisrayeli abwezera cilango pfuko la Benjamini 1 Pamenepo anaturuka ana onse a Israyeli, nuunjikana msonkhano kwa Yehova ku Mizipa ngati munthu mmodzi, kuyambira ku Dani mpaka Beereseba ndi dziko la…

Oweruza 21

Pfuko la Benjamini limangidwanso 1 Koma amuna a Israyeli adalumbira ku Mizipa, ndi kuti, Palibe mmodzi wa ife adzapereka mwana wace wamkazi kwa Mbenjamini akhale mkazi wace. 2 Ndipo anthu…

Rute 1

Naomi ndi apongozi ace awiri 1 NDIPO masiku akuweruza oweruzawo munali njala m’dziko. Ndipo munthu wa ku Betelehemu-Yuda anamuka nakagonera m’dziko la Moabu, iyeyu, ndi mkazi wace, ndi ana ace…

Rute 2

Rute akunkha m’munda wa Boazi 1 Ndipo Naomi anali nave mbale wa mwamuna wace, ndiye munthu mwini cuma cambiri wa banja la Elimeleki; dzina lace ndiye Boazi. 2 Nati Rute…

Rute 3

Boazi anena za kumuombolera Rute colowa 1 Pamenepo Naomi mpongozi wace ananena naye, Mwana wanga, kodi ndisakufunire popumulako, kuti ukhale bwino? 2 Nanga Boazi wodziwana nafe, amene unakhala nao adzakazi…

Rute 4

Boazi akwatira Rute nabadwa Obedi 1 Ndipo Boazi anakwera kumka kucipata, nakhala pansi pomwepo; ndipo taona, woombolera winayo adanena Boazi analinkupita; nati iye, Iwe uje, pambuka, khala pansi apa; napambuka…

1 Samueli 1

1 NDIPO panali munthu wina wa ku Ramatayimu Zofimu, wa dziko la mapiri la Efraimu, dzina lace ndiye Elikana, mwana wace wa Yerohamu, mwana wa Elihu, mwana wa Tohu, mwana…

1 Samueli 2

Coyamikira ca Hana 1 Ndipo Hana anapemphera, nati Mtima wanga umyuka mokondwera kwa Yehova, Nyanga yanga yakwezeka mwa Yehova; Pakamwa panga pakula kwa adani anga; Popeza ndikondwera m’cipulumutsocanu. 2 Palibe…

1 Samueli 3

Masomphenya a Samueli 1 Ndipo mwanayo Samueli anatumikira Yehova pamaso pa Eli. Ndipo masiku aja mau a Yehova anamveka kamodzi kamodzi; masomphenya sanaoneka-oneka. 2 Ndipo kunali nthawi yomweyo Eli atagona…

1 Samueli 4

Afilisti akantha Aisrayeli 1 Ndipo mau a Samueli anafikira kwa Aisrayeli onse. Ndipo Aisrayeli anaturuka kukaponyana nkhondo ndi Afilisti, namanga zithando zao ku Ebenezeri; Afilistiwo namanga m’Afeki. 2 Ndipo Afilistiwo…