Yoswa 14

Kalebe alandira Hebroni 1 Ndipo awa ndi maiko ana a Israyeli anawalanda m’dziko la Kanani, amene Eleazare wansembe, ndi Yoswa mwana wa Nuni, ndi akulu a nyumba za atate a…

Yoswa 15

Malire a Yuda 1 Ndipo gawo la pfuko la ana a Yuda monga mwa mabanja ao linafikira malire a Edomu, ku cipululu ca Zini kumwera, ku malekezero a kumwera. 2…

Yoswa 16

Malire a Efraimu 1 Ndipo gawo La ana a Yosefe linaturuka kucokera ku Yordano ku Yeriko, ku madzi a Yeriko kum’mawa, kucipululu, nakwera kucokera ku Yeriko kumka kumapiri ku Beteli;…

Yoswa 17

Malire a Manase 1 Gawo la pfuko la Manase ndi ili: pakuti anali woyamba wa Yosefe. Makiri mwana woyamba wa Manase, atate wa Gileadi, popeza ndiye munthu wa nkhondo, anakhala…

Yoswa 18

Autsa cihema ku Silo 1 Ndipo msonkhano wonse wa ana a Israyeli unasonkhana ku Silo, nuutsa komweko cihema cokomanako; ndipo dziko linawagoniera. 2 Ndipo anatsala mwa ana a Israyeli mapfuko…

Yoswa 19

Malire a Simeoni 1 Ndipo maere aciwiri anamturukira Simeoni, pfuko la ana a Simeoni monga mwa mabanja ao; ndi colowa cao cinali pakati pa colowa ca ana a Yuda. 2…

Yoswa 20

Midzi yopulumukirako 1 Ndipo Yehova anati kwa Yoswa, 2 Nena ndi ana a Israyeli ndi kuti, Mudziikire midzi yopulumukirako, monga ndinanena kwa inu mwa dzanja la Mose, 3 kuti athawireko…

Yoswa 21

Midzi yokhalamo Alevi 1 Pamenepo akuru a nyumba za atate a Alevi anayandikira kwa Eleazare wansembe, ndi kwa Yoswa mwana wa Nuni, ndi kwa akuru a nyumba za atate a…

Yoswa 22

A pfuko la Rubeni, la Gadi, ndi la Manase logawika pakati, amuka kwao kum’mawa kwa Yordano 1 Pamenepo Yoswa anaitana Arubeni ndi Agadi, ndi pfuko la Manase logawika pakati, 2…

Yoswa 23

Yoswa acenjeza anthu asunge Malamulo a Mulungu 1 Ndipo atapita masiku ambiri, Yehova atapumulitsa Israyeli kwa adani ao onse akuwazungulira, ndipo Yoswa adakalamba nakhala wa zaka zambiri; 2 Yoswa anaitana…