Genesis 11

Nsanja ya Babele 1 Ndipo dziko lapansi linali la cinenedwe cimodzi ndi cilankhulidwe cimodzi. 2 Ndipo panali pamene anayendayenda ulendo kum’mawa, anapeza cigwa m’dziko la Sinara, ndipo anakhala kumeneko. 3…

Genesis 12

Kuitanidwa kwa Abramu 1 Ndipo Yehova anati kwa Abramu, Turuka iwe m’dziko lako, ndi kwa abale ako, ndi ku nyumba ya atate wako, kunka ku dziko limene ndidzakusonyeza iwe; 2…

Genesis 13

Abramu ndi Loti alekana 1 Ndipo anakwera Abramu kucoka ku Aigupto, iye ndi mkazi wace, ndi zonse anali nazo, ndi Loti pamodzi naye, kunka ku dziko la kumwera. 2 Ndipo…

Genesis 14

Abramu alanditsa Loti 1 Ndipo panali masiku a Amarafele mfumu ya Sinara, ndi Arioki mfumu ya Elasara, ndi Kedorelaomere mfumu ya Elami, ndi Tidala mfumu ya Goimu, 2 iwo anathira…

Genesis 15

Mulungu apangana ndi Abramu 1 Zitapita izo, mau a Yehova anadza kwa Abramu m’masomphenya, kuti, Usaope, Abramu, Ine ndine cikopa cako ndi mphotho yako yaikurukuru. 2 Ndipo Abramu anati, Ambuye…

Genesis 16

Sara ndi Hagara 1 Ndipo Sarai mkazi wace wa Abramu sanambalire iye mwana; ndipo anali ndi mdzakazi, wa ku Aigupto, dzina lace Hagara. 2 Ndipo Sarai anati kwa Abramu, Taonanitu,…

Genesis 17

Dzina la Abramu lisinthika likhale Abrahamu 1 Pamene Abramu anali wa zaka makumi asanu ndi anai kudza zisanu ndi zinai, Yehova anamuonekera Abramu nati kwa iye, Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse;…

Genesis 18

Amithenga atatu amuonekera Abrahamu 1 Ndipo Yehova anamuonekera iye pa mtengo yathundu ya ku Mamre, pamene anakhala pa khomo la hema wace pakutentha dzuwa. 2 Ndipo anatukula maso ace, nayang’ana,…

Genesis 19

Cionongeko ca Sodomu ndi Gomora 1 Ndipo anadza ku Sodomu madzulo amithenga awiri; ndipo Loti anakhala pa cipata ca Sodomu, ndipo Loti anaona iwo, nauka kuti akakomane nao, ndipo anaweramitsa…

Genesis 20

Abrahamu kwa mfumu Abimeleke 1 Abrahamu ndipo anacoka kumeneko kunka ku dziko la kumwera, ndipo anakhala pakati pa Kedesi ndi Suri, ndipo anakhala ngati mlendo m’Gerari. 2 Ndipo Abrahamu anati…