Deuteronomo 28

Madalitso pa kumvera kwao 1 Ndipo kudzali, mukadzamvera mau a Yehova Mulungu wanu mwacangu, ndi kusamalira kucita malamulo ace onse amene ndikuuzani lero, kuti Yehova Mulungu wanu adzakukulitsani koposa amitundu…

Deuteronomo 29

Mulungu abwereza kupangana nao 1 Awa ndi mau a cipangano cimene Yehova analamulira Mose acicite ndi ana a Israyeli m’dziko la Moabu, pamodzi ndi cipanganoco anacita nao m’Horebe. 2 Ndipo…

Deuteronomo 30

Mulungu alonjeza kuwalanditsa akalapa atacimwa 1 Ndipo kudzakhala, zikakugwerani zonsezi, mdalitso ndi temberero, ndinaikazi pamaso panu, ndipo mukazikumbukila mumtima mwanu mwa amitundu onse, amene Yehova Mulungu wanu anakupitikitsiraniko; 2 nimukabwerera…

Deuteronomo 31

Yoswa adzalowa m’malo a Mose 1 Ndipo Mose anamuka nanena mau awa kwa Israyeli wonse, 2 nati nao, Ndine munthu wa zaka zana ndi makumi awiri lero lino; sindikhozanso kuturuka…

Deuteronomo 32

Nyimbo adailemba Mose 1 Kumwamba kuchere khutu, ndipo ndidzanena; Ndi dziko lapansi limve mau a m’kamwa mwanga; 2 Ciphunzitso canga cikhale ngati mvula; Maneno anga agwe ngati mame; Ngati mvula…

Deuteronomo 33

Mose adalitsa mafuko 12 a Israyeli asanafe 1 Ndipo mdalitso, Mose munthu wa Mulungu anadalitsa nao ana a Israyeli asanafe, ndi uwu. 2 Ndipo anati, Yehova anafuma ku Sinai, Nawaturukiraku…

Deuteronomo 34

1 Ndipo Mose anakwera kucokera ku zidikha za Moabu, kumka ku phiri la Nebo, pamwamba pa Pisiga, popenyana ndi Yeriko. Ndipo Yehova anamuonetsa dziko lonse la Gileadi, kufikira ku Dani;…

Yoswa 1

1 NDIPO atafa Mose mtumiki wa Yehova, Yehova anati kwa Yoswa mwana wa Nuni mnyamata wa Mose, 2 Mose mtumiki wanga wafa; tauka tsono, nuoloke Yordano uyu, iwe ndi anthu…

Yoswa 2

Yoswa atuma anthu awiri azonde Yeriko 1 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni, ali ku Sitimu, anatuma amuna awiri mosadziwika kukazonda, ndi kuti, Mukani, mulipenye dzikolo, ndi ku Yeriko. Ndipo anamuka…

Yoswa 3

Aisrayeli aoloka Yordano 1 Ndipo Yoswa analawirira mamawa, kucoka ku Sitimu, nafika ku Yordano, iye ndi ana onse a Israyeli; nagona komweko, asanaoloke. 2 Ndipo kunali atapita masiku atatu, akapitao…