Deuteronomo 18
Zoyenera ansembe ndi Alevi 1 Ansembe Alevi, pfuko lonse la Levi, alibe gawo kapena colowa pamodzi ndi Israyeli; azizidya nsembe zamoto za Yehova, ndi colowa cace, 2 Alibe colowa pakati…
Zoyenera ansembe ndi Alevi 1 Ansembe Alevi, pfuko lonse la Levi, alibe gawo kapena colowa pamodzi ndi Israyeli; azizidya nsembe zamoto za Yehova, ndi colowa cace, 2 Alibe colowa pakati…
Za midzi yopulumukirako 1 Pamene Yehova Mulungu wanu ataononga amitundu, amene Yehova Mulungu wanu akupatsani dziko lao, ndipo mutalilandira lanu lanu, ndi kukhala m’midzi mwao, ndi m’nyumba zao; 2 pamenepo…
Malamulo a kunkhondo 1 Pamene muturuka pa mdani wanu kunkhondo, ndi kuona akavalo ndi magareta ndi anthu akucurukira inu, musawaopa; popeza Yehova Mulungu wanu, amene anakukwezani kukuturutsani m’dziko la Aigupto,…
Za wophedwa mosadziwika 1 Akapeza munthu waphedwa m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani likhale lanu lanu, nagona pamunda, wosadziwika wakumkantha, 2 pamenepo azituruka akuru anu ndi oweruza anu, nayese ku…
Za zoweta zolowerera 1 Mukapenya ng’ombe kapena nkhosa ya mbale wako zirikusokera musamazilekerera, muzimbwezera mbale wanu ndithu. 2 Ndipo ngati mbale wanu sakhala pafupi ndi inu, kapena mukapanda kumdziwa, mubwere…
Oletsedwa ku msonkhano wa Yehova 1 Munthu wophwetekwa, wophwanyika kapena wofulika, asalowe m’msonkhano wa Yehova. 2 Mwana wa m’cigololo asalowe m’msonkhano wa Yehova, ngakhale mbadwo wace wakhumi usalowe m’msonkhano wa…
Za kalata wa cilekaniro, cikole, kuba munthu, khate 1 Munthu akatenga mkazi akhale wace, kudzali, ngati sapeza ufulu pamaso pace, popeza anapeza mwa iye kanthu kosayenera, amlembere kalata wa cilekanitso,…
Za makwapulidwe a wolakwa 1 Pakakhala ndeu pakati pa anthu, nakapita kukaweruzidwa iwowa, nakaweruza mlandu wao oweruza; azimasula wolungama, namange woipa. 2 Ndipo kudzali, wocita coipa akayenera amkwapule, woweruza amgonetse…
Copereka ca zipatso zoyamba 1 Ndipo kudzali, utakalowa m’dziko limene Yehova Mulungu wanu akupatsani likhale colowa canu, ndipo mwacilandira ndi kukhala m’mwemo; 2 kuti muzitengako zoyamba za zipatso zonse za…
Za kuutsa miyala va cikumbutso ataoloka Yordano 1 Ndipo Mose ndi akuru a Israyeli anauza anthu, nati, Sungani malamulo onse ndikuuzani lero. 2 Ndipo kudzali, tsiku lakuoloka inu Yordano kulowa…