Numeri 24

1 Pamene Balamu anaona kuti kudakomera pamaso pa Yehova kudalitsa Israyeli, sanamuka, monga nthawi zija zina, ku nyanga zolodzera, koma anayang’ana nkhope yace kucipululu. 2 Ndipo Balamu anakweza maso ace,…

Numeri 25

Aisrayeli acita cigololo napembedza mafano ku Sitimu 1 Ndipo Israyeli anakhala m’Sitimu, ndipo anthu anayamba kucita cigololo ndi ana akazi a Moabu; 2 popeza anaitana anthuwo adze ku nsembe za…

Numeri 26

Awerenzedwa Aisrayeli 1 Ndipo kunali, utatha mliriwo, Yehova ananena ndi Mose ndi Eleazara mwana wa Aroni wansembe, nati, 2 Werenga khamu lonse la ana a Israyeli, kuyambira a zaka makumi…

Numeri 27

Ana akazi a Tselofekadi 1 Pamenepo anayandikiza ana akazi a Tselofekadi mwana wa Heferi, ndiye mwana wa Gileadi, ndiye mwana wa Makiri, ndiye mwana wamwamuna wa Manase, wa mabanja a…

Numeri 28

Nsembe yopsereza yosalekeza 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Uza ana a Israyeli, nuti nao, Muzisamalira kubwera naco kwa Ine copereka canga, cakudya canga ca nsembe zanga zamoto,…

Numeri 29

1 Ndipo mwezi wacisanu ndi ciwiri, tsiku loyamba la mweziwo, muzikhala nako kusonkhana kopatulika; musamacita nchito ya masiku ena; likukhalireni inu tsiku lakuliza malipenga. 2 Pamenepo muzipereka nsembeyopsereza ya pfungo…

Numeri 30

Za cowinda cocita akazi 1 Ndipo Mose ananena ndi akuru a mapfuko a ana a Israyeli, nati, Cinthu anacilamulira Yehova ndi ici: 2 Munthu akacitira Yehovacowinda, kapena akalumbira lumbiro ndi…

Numeri 31

Aisrayeli agonjetsa Amidyani 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Abwezereni cilango Amidyani cifukwa ca ana a Israyeli; utatero udzaitanidwa kumka kwa anthu a mtundu wako. 3 Ndipo Mose…

Numeri 32

Arubeni, Agadi, ndi Amanase alandira colowa cao tsidya lino la Yordano 1 Koma ana a Rubeni ndi ana a Gadi anali nazo zoweta zambirimbiri; ndipo anapenyerera dziko la Yazeri, ndi…

Numeri 33

Za ulendo wa Aisrayeli pakati pa Ramese ndi Sitimu 1 Maulendo a ana a Israyeli amene anaturuka m’dziko la Aigupto monga mwa makamu ao, ndi dzanja la Mose ndi Aroni,…