Numeri 14
Aisrayeli afuna kubwerera kumka ku Aigupto 1 Pamenepo khamu lonse linakweza mau ao, napfuula; ndipo anthuwo analira usikuwo. 2 Ndipo ana onse a Israyeli anadandaulira Mose ndi Aroni; ndi khamu…
Aisrayeli afuna kubwerera kumka ku Aigupto 1 Pamenepo khamu lonse linakweza mau ao, napfuula; ndipo anthuwo analira usikuwo. 2 Ndipo ana onse a Israyeli anadandaulira Mose ndi Aroni; ndi khamu…
Malamulo a pa nsembezo 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose nati, 2 Nena ndi ana a Israyeli, nuti nao, Mukakalowa m’dziko lokakhalamo inu, limene ndirikupatsa inu, 3 ndipo mukakonzera Yehova…
Kora, Datani, ndi Abiramu aukira Mose 1 Koma Kora, mwana wa Izara, mwana wa Kohati, mwana wa Levi, anatenga Datani ndi Abiramu, ana a Eliyabu, ndi Oni mwana wa Peleti,…
Ndodo ya Aroni iphuka 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Nena ndi ana a Israyeli, nulandire kwa yense ndodo, banja liri onse la makolo ndodo imodzi, mafuko ao…
Udindo wa ansembe ndi Alevi, ndi zolandira zao 1 Ndipo Yehova anati kwa Aroni, Iwe ndi ana ako amuna ndi banja la kholo lako pamodzi ndi iwe muzisenza mphulupulu ya…
Za ng’ombe yamsoti yofiira ndi madzi oyeretsa nao 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, nati, 2 Ili ndi lemba la cilamulo Yehova adalamuliraci, ndi kuti, Nena ndi ana…
Imfa ya Miriamu; madzi a Meriba 1 Ndipo ana a Israyeli, ndilo khamu lonse, analowa m’cipululu ca Zini mwezi woyamba; ndipo anthu anakhala m’Kadesi; kumeneko anafa Miriamu, naikidwakomweko. 2 Ndipo…
Aisrayeli aononga Akanani 1 Pamene Mkanani, mfumu ya Aradi, wokhala kumwela, anamva kuti Israyeli anadzera njira ya azondi, anathira nkhondo pa Israyeli, nagwira ena akhale ansinga. 2 Ndipo Israyeli analonjeza…
Za Balamu ndi Balaki 1 Ndipo ana a Israyeli anayenda ulendo, namanga mahema m’zigwa za Moabu, tsidya la Yordano ku Yeriko. 2 Ndipo Balaki mwana wa Zipori anaona zonse Israyeli…
1 Ndipo Balamu anati kwa Balaki, Ndimangireni kuno maguwa a nsembe asanu ndi awiri, nimundikonzere kuno ng’ombe zisanu ndi ziwiri, ndi nkhosa zamphongo zisanu ndi ziwiri. 2 Ndipo Balaki anacita…