Numeri 4

Akohati 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose ndi Aroni, nati, 2 Werengani ana a Kohati pakati pa ana a Levi, monga mwa mabanja ao, monga mwa nyumba za makolo ao,…

Numeri 5

Odetsedwa onse acotsedwe kucigono 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, 2 Uza ana a Israyeli kuti aziturutsa m’cigono akhate onse, ndi onse akukhala nako kukha, ndi onse odetsedwa…

Numeri 6

Za cowinda ca Mnaziri 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Nena ndi ana a Israyeli, nuti nao, Mwamuna kapena mkazi akadzipatulira kulonieza cowinda ca Mnaziri, kudzipatulira kwa Yehova;…

Numeri 7

Zopereka za Akuru 12 atautsa cihemaco 1 Ndipo kunali kuti tsiku lomwe Mose anatsiriza kumuutsa kacisi, namdzoza ndi kumpatula, ndi zipangizo zace zonse, ndi guwa la nsembe, ndi zipangizo zace…

Numeri 8

Za kuyatsa nyalizo 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Nena kwa Aroni, nuti naye, Pamene uyatsa nyalizo, nyali manu ndi ziwirizo ziwale pandunji pace pa coikapo nyalico. 3…

Numeri 9

Acita Paskha 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose m’cipululu ca Sinai, mwezi woyamba wa caka caciwiri ataturuka m’dziko la Aigupto, ndi kuti, 2 Ana a Israyeli acite Paskha pa nyengo…

Numeri 10

Adzipangira malipenga awiri asiliva 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Dzipangire malipenga awiri asiliva; uwasule mapangidwe ace; ucite nao poitana khamu, ndi poyendetsa a m’zigono. 3 Akaliza, khamu…

Numeri 11

Kudandaula kwa Aisrayeli 1 Ndipo anthu anaipa, namadandaula m’makutu a Yehova; ndipo pamene Yehova anamva anapsa mtima; ndi mota wa Yehova unayaka pakati pao, nunyeketsa ku cilekezero ca cigono. 2…

Numeri 12

Miriamu ndi Aroni aukira Mose 1 Ndipo Miriamu ndi Aroni anatsutsana naye Mose cifukwa ca mkazi mtundu wace Mkusi amene adamtenga; popeza adatenga mkazi Mkusi. 2 Ndipo anati, Kodi Yehova…

Numeri 13

Atumidwa amuna 12 kukazonda Kanani 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Udzitumire amuna, kuti azonde dziko la Kanani, limene ndirikupatsa ana a Israyeli; utumize munthu mmodzi wa pfuko…