Cibvumbulutso 14

Mwanawankhosa ndi oomboledwa ace pa phiri la Ziyoni 1 Ndipo ndinapenya, taonani, Mwanawankhosayo alikuimirira pa phiri la Ziyoni, ndipo pamodzi ndi iye zikwi zana mphambu makumi anai kudza anai, akukhala…

Cibvumbulutso 15

Angelo asanu ndi awiri ndi miliri isanu ndi iwiri 1 Ndipo ndinaona cizindikilo cina m’mwamba, cacikuru ndi cozizwitsa, angelo asanu ndi awiri akukhala nayo miliri isanu ndi iwiri, ndiyo yotsiriza,…

Cibvumbulutso 16

1 Ndipo ndinamva mau akuru ocokera kuKacisi, akunena kwa angelo asanu ndi awiri, Mukani, ndipo tsanulirani kudziko mbale zisanu ndi ziwiri za mkwiyo wa Mulungu. 2 Ndipo anacoka woyamba, natsanulira…

Cibvumbulutso 17

Kupasuka kwa Babulo. Cirombo cisokeretsa mkazi wacigololo 1 Ndipo anadza mmodzi mwa angelo asanu ndi awiri akukhala nazo mbale zisanu ndi ziwiri, nalankhula ndi ine, nanena, Idza kuno, ndidzakuonetsa citsutso…

Cibvumbulutso 18

Kupasuka kwa Babulo. Maliro pa dziko lapansi 1 Zitatha izi ndinaona mngelo wina wakutsika m’Mwamba wakukhala nao ulamuliro waukuru; ndipo dziko linaunikidwa ndi ulemerero wace. 2 Ndipo anapfuula ndi mau…

Cibvumbulutso 19

Kupasuka kwa Babula. Cimwemwe ndi mayamiko m’Mwamba 1 Zitatha izi ndinamva ngati a mau akuru khamu lalikuru m’Mwamba, liri kunena, Aleluya; cipulumutso, ndi ulemerero, ndi mphamvu, nza Mulungu wathu; 2…

Cibvumbulutso 20

Satana womangidwa zaka cikwi 1 Ndipo ndinaona mngelo anatsika Kumwamba, nakhala naco cifungulo ca phompho, ndi unyolo waukuru m’dzanja lace. 2 Ndipo anagwira cinjoka, njoka yakaleyo, ndiye mdierekezi ndi Satana,…

Cibvumbulutso 21

Miyamba yatsopano ndi dziko latsopano 1 Ndipo ndinaona m’mwamba mwatsopano ndi dziko latsopano; pakuti m’mwamba moyamba ndi dziko loyamba zidaeoka, ndipo kulibenso nyanja. 2 Ndipo ndinaona mzinda woyerawo, Yerusalemu watsopano,…

Cibvumbulutso 22

1 Ndipo anandionetsa mtsinje wa madzi a moyo, wonyezimira ngati krustalo, oturuka ku mpando wacifumu wa Mulungu ndi wa Mwanawarikhosa. 2 Pakati pa khwalala lace, ndi tsidya ili la mtsinje,…