Cibvumbulutso 4

Masomphenya a mpando wacifumu wa Mulungu, akuru makumi awiri ndi anai, ndi zamoyo zinai 1 Zitatha izi ndinapenya, ndipo taonani, khomo lotseguka m’Mwamba, ndipo mau oyamba ndinawamva, ngati lipenga Iakulankhuia…

Cibvumbulutso 5

Buku losindikizika ndi zosindikiza zisanu ndi ziwiri. Mwanawankhosa yekha ayenera kulitsegula 1 Ndipo ndinaona m’dzanja lamanja la iye wakukhala pa mpando wacifumu buku lolembedwa m’kati ndi kunja kwace, losindikizika ndi…

Cibvumbulutso 6

Atsegula zosindikiza zisanu ndi cimodzi 1 Ndipo ndinaona pamene Mwanawankhosa anamasula cimodzi ca zizindikilo zisanu ndi ziwiri, ndipo ndinamva cimodzi mwa zamoyo zinai, nicinena, ngati mau a bingu, Idza. 2…

Cibvumbulutso 7

Aisrayeli okhulupirika alanditsidwa 1 Zitatha izi ndinao na angelo anai alinkuimirira pa ngondya zinai za dziko, akugwira mphepo zinai za dziko, kuti ingaombe mphepo padziko, kapena panyanja, kapena pa mtengo…

Cibvumbulutso 8

Atsegula cosindikiza cacisanu ndi ciwiri. Angelo asanu ndi awiri, ndi malipenga oyamba anai 1 Ndipo pamene anamasula cizindikilo cacisanu ndi ciwiri, munali cete m’Mwamba monga mwa nthawi ya ora latheka….

Cibvumbulutso 9

Lipenga lacisanu, tsoka loyamba 1 Ndipo mngelo wacisanu anaomba, ndipo ndinaona nyenyezi yocokera kumwamba idagwa padziko; ndipo anampatsa iye cifunguliro ca dzenje la phompho. 2 Ndipo anatsegula pa dzenje la…

Cibvumbulutso 10

Yohane adya buku locokera Kumwamba 1 Ndipo ndinaona mngelo wina wolimba alikutsika Kumwamba, wobvala mtambo; ndi utawaleza pamutu pace, ndi nkhope yace ngati dzuwa, ndi mapazi ace ngati mizati yamoto;…

Cibvumbulutso 11

Mboni ziwirt 1 Ndipoanandipatsa ine bango ngati ndodo, ndikuti, Tanyamuka, nuyese Kacisi wa Mulungu, ndi guwa la nsembe, ndi iwo akulambiramo. 2 Ndipo bwalo la kunja kwa Kacisi ulisiye padera,…

Cibvumbulutso 12

Za mkazi ndi cinjoka 1 Ndipo cizindikilo cacikuru cinaoneka m’mwamba; mkazi wobvekedwa dzuwa, ndi mwezi ku mapazi ace, ndi pamutu pace korona wa nyenyezi khumi ndi ziwiri; 2 ndipo anali…

Cibvumbulutso 13

Cirombo cakuturuka m’nyanja 1 Ndipo ndinaimirira pa mcenga wa nyanja. Ndipo ndinaona cirombo cirinkuturuka m’nyanja, cakukhala nazo nyanga khumi, ndi mitu isanu ow iwiri, ndi pa nyanga zace nduwira zacifumu…