1 Yohane 2
1 Tiana tanga, izi ndikulemberani, kuti musacimwe. Ndipo akacimwa wina, Nkhoswe tiri naye kwa Atate, ndiye Yesu Kristu wolungama; 2 ndipo iye ndiye ciombolo ca macimo athu; koma wosati athu…
1 Tiana tanga, izi ndikulemberani, kuti musacimwe. Ndipo akacimwa wina, Nkhoswe tiri naye kwa Atate, ndiye Yesu Kristu wolungama; 2 ndipo iye ndiye ciombolo ca macimo athu; koma wosati athu…
Ife ndife ana a Mulungu 1 Taonani, cikondico Atate watipatsa, kuti tichedwe ana a Mulungu; ndipo tiri ife otere. Mwa ici dziko lapansi silizindikira ife, popeza silimzindikira iye. 2 Okondedwa,…
Za aphunzitsi onyenga 1 Okondedwa, musamakhulupirira mzimu uli wonse, koma yesani mizimu ngati icokera mwa Mulungu: popeza aneneri onyenga ambiri anaturuka kulowa m’dziko lapansi. 2 M’menemo muzindikira Mzimu Wl Mulungu:…
Za kukhulupirira Yesu ndi zotsatira zace 1 Yense wokhulupirira kuti Yesu ndiye Kristu wabadwa kucokera kwa Mulungu; ndipo yense wakukonda iye amene anabala akondanso iye amene anabadwa wocokera mwa iye….
1 MKURUYO kwa mkazi womveka wosankhika, ndi ana ace, amene ine ndikondana nao m’coonadi; ndipo si ine ndekha, komanso onse akuzindikira coonadi; 2 cifukwa ca coonadi cimene cikhala mwa ife,…
1 MKURUYO kwa Gayo wokondedwayo, amene ndikondana naye m’coonadi. 2 Wokondedwa, ndipemphera kuti pa zonse ulemere, nukhale bwino, monga mzimu wako ulemera, 3 Pakuti ndinakondwera kwakukuru, pofika abale ndi kucita…
1 YUDA, kapolo wa Yesu Kristu, ndi mbale wa Yakobo, kwa iwo oitanidwa, okondedwa mwa Mulungu Atate, ndi osungidwa ndi Yesu Kristu: 2 Cifundo ndi mtendere ndi cikondi zikucurukireni. Atsutsa…
Coneneratu bukuli 1 CIBVUMBULUTSO ca Yesu Kristu, cimene Mulungu anambvumbulutsira acionetsere akapolo ace, ndico ca izi ziyenera kucitika posacedwa: ndipo potuma mwa mngelo wace anazindikiritsa izi kwa kapolo wace Yohane;…
Kalata wa kwa Mpingo wa ku Efeso 1 Kwa mngelo wa Mpingo wa ku Efeso lemba; Izi azinena iye amene agwira nyenyezi zisanu ndi ziwiri m’dzanja lace lamanja, iye amene…
Kalata wacisanu, wa kwa Mpingo wa ku Sarde 1 Ndipo kwa mngelo wa Mpingo wa ku Sarde lemba: Izi anena iye wakukhala nayo mizimu isanu ndi iwiri ya Mulungu, ndi…