Yakobo 5

Acuma ouma mtima atsutsidwa 1 Nanga tsono acuma inu, lirani ndi kucema cifukwa ca masautso anu akudza pa inu, 2 Cuma canu caola ndi zobvala zanu zajiwa ndi njenjete. 3…

1 Petro 1

1 PETRO, mtumwi wa Yesu Kristu, kwa osankhidwa akukhala: alendo a cibalaliko a ku Ponto, Galatiya, Kapadokiya, Asiya, ndi Bituniya, 2 monga mwa kudziwiratu kwa Mulungu Atate, m’ciyeretso ca Mzimu,…

1 Petro 2

1 Momwemo pakutaya coipa conse, ndi cmyengo conse, ndi maonekedwe onyenga, ndi kadoka, ndi masiniiriro onse, 2 lirani monga makanda alero mkaka woyenera, wopanda cinyengo, kuti mukakule nao kufikira cipulumutso;…

1 Petro 3

Zoyenera akazi ndi amuna 1 Momwemonso, akazi inu, mverani amuna anu ainu nokha; kuti, ngatinso ena samvera mau, akakodwe opanda mau mwa mayendedwe a akazi; 2 pakuona mayendedwe anu oyera…

1 Petro 4

1 Popeza Kristu adamva zowawa m’thupi, mudzikonzere mtima womwewo; pakuti iye amene adamva zowawa m’thupi walekana nalo cimo; 2 kuti nthawi yotsalira simukakhalenso ndi moyo m’thupi kutsata zilakolako za anthu,…

1 Petro 5

Zoyenera akulu ndi anyamata; adzicepetse, adikire 1 Akulu tsono mwa inu ndiwadandaulira, ine mkulu mnzanu ndi mboni ya zowawa za Kristu, ndinenso wolawana nao ulemerero udzabvumbulutsikawo: 2 Wetani gulu la…

2 Petro 1

1 SIMONI Petro, kapolo ndi mtumwi wa Yesu Kristu kwa iwo amene adalandira cikhulupiriro ca mtengo wace womwewo ndi ife, m’cilungamo ca Mulungu wathu ndi Mpulumutsi Yesu Kristu: 2 Cisomo…

2 Petro 2

Za aphunzitsi onyenga 1 Koma padakhalanso pakati pa anthuwo aneneri onama, monganso padzakhala aphunzitsi onama pakati pa inu, amene adzalowa nayo m’tseri mipatuko yotayikitsa, nadzakana Ambuye amene adawagula, nadzadzitengera iwo…

2 Petro 3

Kubwera kwa Ambuye 1 Okondedwa, uyu ndiye kalata waciwiri ndilembera kwa inu tsopano; mwa onse awiri nditsitsimutsa mtima wanu woona ndi kukukumbutsani; 2 kuti mukumbukile mau onenedwa kale ndi aneneri…

1 Yohane 1

Mau a moyo aoneka m’thupi 1 CIMENE cinaliko kuyambira paciyambi, cimene tidacimva, cimene tidaciona m’maso mwathu, cimene tidacipenyerera, ndipo manja athu adacigwira ca Mau a moyo, 2 (ndipo moyowo unaonekera,…