Ahebri 8
Cipangano cakale ndi cofanizira ndi copita, Kristu ali Nkhoswe ya cipangano cosatha 1 Koma mutu wafzi tanenazi ndi uwu: Tiri naye Mkuruwansembe wotere, amene anakhala pa dzanja lamanja la mpando…
Cipangano cakale ndi cofanizira ndi copita, Kristu ali Nkhoswe ya cipangano cosatha 1 Koma mutu wafzi tanenazi ndi uwu: Tiri naye Mkuruwansembe wotere, amene anakhala pa dzanja lamanja la mpando…
Nsembe za’cipangano cakale zidacitika kawiri kawiri, nsembe ya Yesu idacitika kamodzi kokha 1 Ndipo cingakhale cipangano coyambaci cinali nazo zoikika za kulambira, ndi malo opatulika a pa dziko lapansi. 2…
Pakuti cilamulo pokhala nao 1 mthunzi wa zokoma zirinkudza, osati cifaniziro ceni ceni ca zinthuzo, sicikhozatu, ndi nsembe zomwezi caka ndi caka, zimene azipereka kosalekeza, kuwayesera angwiro iwo akuyandikira. 2…
Mtima wa cikhulupiriro. Okhulupirira a m’Cipangano cakale 1 Koma cikhulupiriro ndico cikhazikitso ca zinthu zoyembekezeka, ciyesero ca zinthu zosapenyeka. 2 Pakuti momwemo akulu anacitidwa umboru. 3 Ndi cikhulupiriro tizindikira kuti…
Tipirire angakhale masautso acuruka, monga anatero Kristu 1 Cifukwa cace ifenso, popeza tizingidwa nao mtambo waukuru wotere wa mboni, titaye colemetsa ciri conse, ndi cimoli Iimangotizinga, ndipo tithamange mwacipiriro makaniwo…
1 Cikondi ca pa abale cikhalebe. 2 Musaiwale kucereza alendo; pakuti mwa ici ena anacereza angelo osacidziwa. 3 Kumbukilani am’nsinga, monga am’nsinga anzao; ocitidwa zoipa, monga ngati inunso adatero nanu…
1 YAKOBO, kapolo wa Mulungu ndi wa Ambuye Yesu Kristu, kwa mafuko khumi ndi awiri a m’cibalaliko: ndikulankhulani. Za mayesero 2 Muciyese cimwemwe cokha, abale anga, m’mene mukugwa m’mayesero a…
Asacite tsankhu pakati pa anthu 1 Abate anga, musakhale naco cikhulupiriro ca Ambuye wathu Yesu Kristu, Ambuye wa ulemerero, ndi kusamala maonekedwe. 2 Pakuti akalowa m’sunagoge mwanu munthu wobvala mphete…
Aziceniera ndi pakamwa pao 1 Musakhale aphunzitsi ambiri, abale anga, podziwa kuti tidzalangika koposa. 2 Pakuti timakhumudwa tonse pa zinthu zambiri. Munthu akapanda kukhumudwa pa mau, iye ndiye munthu wangwiro,…
Adziletse polakalaka zoipa 1 Zicokera kuti nkhondo, zicokera kuti zolimbana mwa inu? Kodi sizicokera ku zikhumbitso zanu zocita nkhondo m’ziwalo zanu? 2 Mulakalaka, ndipo zikusowani; mukupha, nimucita kaduka, ndipo simukhoza…