Tito 2

Maceniezedwe a okalamba ndi anyamata ndi akapolo. Akhale citsanzo yekha Tito 1 Koma iwe, lankhula zimene ziyenera ciphunzitso colamitsa: 2 okalamba akhale odzisunga, olemekezeka, odziletsa, olama m’cikhulupiriro, m’cikondi, m’cipiriro. 3…

Tito 3

1 Uwakumbutse iwo agonje kwa akulu, ndi aulamuliro, akhale omvera, okonzeka pa nchito iri yonse yabwino; 2 asacitire mwano munthu ali yense, asakhale andeu, akhale aulere, naonetsere cifatso conse pa…

Filemoni 1

1 PAULO, wandende wa Kristu Yesu, ndi Timoteo mbaleyo, kwa Filemoni wokondedwayo ndi wanchito mnzathu, 2 ndi kwa Apiya mlongoyo, ndi Arkipo msilikari mnzathu, ndi kwa Mpingo uli m’nyumba yako;…

Ahebri 1

Kristu Mwana wa Mulungu aposatu angelo 1 KALE Mulungu analankhula ndi makolo mwa aneneri m’manenedwe ambiri ndi mosiyana-siyana, 2 koma pakutha pace pa masiku ano analankhula ndi ife ndi Mwana…

Ahebri 2

Yesu Kristu Nkhoswe yathu yakuposa angelo akhoza kumva nate cifundo 1 Mwa ici tiyenera kusamaliradi zimene tidazimvazi kuti kapena tingatengedwe ndi kusiyana nazo. 2 Pakuti ngati mau adalankhulidwa ndi angelo…

Ahebri 3

Kristu ali wamkuru woposa Mose, Awacenjeza amkhulupirire 1 Potero, abale oyera mtima, olandirana nao maitanidwe akumwamba, lingirirani za Mtumwi ndi. Mkuluwansembe wa cibvomerezo cathu, Yesu; 2 amene anakhala wokhulupirika kwa…

Ahebri 4

1 Cifukwa cace tiope kuti kapena likatsala lonjezano lakulowa mpumulo wace, wina wa inu angaoneke ngati adaliperewera. 2 Pakuti kwa ifenso walalikidwa Uthenga Wabwino, monganso kwa iwo; koma iwowa sanapindula…

Ahebri 5

1 Pakuti mkulu wa ansembe ali yense, wotengedwa mwa anthu, amaikika cifukwa ca anthu m’zinthu za kwa Mulungu, kuti apereke mitulo, ndiponso nsembe, cifukwa ca macimo: 2 akhale wokhoza kumva…

Ahebri 6

1 Mwa ici, polekana nao mau a ciyambidwe ca Kristu, tipitirire kutsata ukulu msinkhu; osaikanso maziko a kutembenuka mtima kusiyana nazo nchito zakufa, ndi a cikhulupiriro ca pa Mulungu, 2…

Ahebri 7

Mkuru wa ansembe Melikizedeke afanizira Yesu Kristu, Mkuruwansembe wosatha 1 Pakuti Melikizedeke uyu, Mfumu ya Salemu, wansembe wa Mulungu Wamkulukulu, amene anakomana ndi Abrahamu, pobwera iye adawapha mafumu aja, namdalitsa,…