Aefeso 4
Umodzi wa iwo a cikhulupiriro 1 Ndikudandaulirani inu tsono, ine wandende mwa Ambuye, muyende koyenera maitanidwe amene munaitanidwa nao, 2 ndi kuonetsera kudzicepetsa konse, ndi cifatso, ndi kuonetsera cipiriro, ndi…
Umodzi wa iwo a cikhulupiriro 1 Ndikudandaulirani inu tsono, ine wandende mwa Ambuye, muyende koyenera maitanidwe amene munaitanidwa nao, 2 ndi kuonetsera kudzicepetsa konse, ndi cifatso, ndi kuonetsera cipiriro, ndi…
1 Cifukwa cace khalani akutsanza a Mulungu, monga ana okondedwa; 2 ndipo yendani m’cikondi monganso Kristu anakukondani inu, nadzipereka yekha m’malo mwathu, copereka ndi nsembe kwa Mulungu, ikhale pfungo lonunkhira…
1 Ananu, mverani akukubalani mwa Ambuye, pakuti ici ncabwino. 2 Lemekeza atate wako ndi amako (ndilo lamulo loyamba lokhala nalo lonjezano), 3 kuti kukhale bwino ndi iwe, ndi kuti ukhale…
1 PAULO ndi Timoteo, akapolo a Yesu Kristu, kwa oyera mtima onse mwa Kristu Yesu, akukhala ku Filipi, pamodzi ndi oyang’anira ndi atumiki: 2 Cisomo kwa inu ndi mtendere za…
1 Ngati tsono muli citonthozo mwa Kristu, ngati cikhazikitso ca cikondi, ngati ciyanjano ca Mzimu, ngati phamphu, ndi zisoni, 2 kwaniritsani cimwemwe canga, kuti mukalingalire mtima zomwezo, akukhala naco cikondi…
A wacenjeza asatsate alum wi onyenga, Aonetsere zipatso za Mzimu 1 Cotsalira, abale anga, kondwerani mwa Ambuye. Kulembera zomwezo kwa inu, sikundibvuta ine, koma kwa inu kuli kukhazikitsa. 2 Penyererani…
1 Potero, abale anga okondedwa, olakalakidwa, ndinu cimwemwe canga ndikorona wanga, cirimikani motere mwa Ambuye, okondedwa. 2 Ndidandaulira Euodiya, ndidandaulira Suntuke, alingirire ndi mtima umodzi mwa Ambuye. 3 Inde, ndikupemphaninso,…
1 PAULO, mtumwi wa Kristu Yesu mwa cifuniro ca Mulungu, ndi Timoteo mbaleyo, 2 kwa oyera mtima ndi abale okhulupirika mwa Kristu a m’Kolose: Cisomo kwa inu ndi mtendere wocokera…
1 Pakuti ndifuna kuti inu mudziwe nkhawa imene ndiri nayo cifukwa ca inu, ndi iwowa a m’Laodikaya, ndi onse amene sanaone nkhope yanga m’thupi; 2 kuti itonthozeke mitima yao, nalumikizike…
Atsate kuyera-mtima, ndi cikondano ca pa abale 1 Cifukwa cace ngati munaukitsidwa pamodzi ndi Kristu, funani zakumwamba, kumene kuli Kristu wokhala pa dzanja lamanja la Mulungu. 2 Lingalirani zakumwamba osati…