2 Akorinto 13
1 Nthawi yacitatu iyi ndirinkudza kwa inu. Pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu maneno onse adzakhazikika. 2 Ndinanena kale, ndipo ndinena ndisanafikeko, monga pamene ndinali pomwepo kaciwiri kaja, pokhala ine…
1 Nthawi yacitatu iyi ndirinkudza kwa inu. Pakamwa pa mboni ziwiri kapena zitatu maneno onse adzakhazikika. 2 Ndinanena kale, ndipo ndinena ndisanafikeko, monga pamene ndinali pomwepo kaciwiri kaja, pokhala ine…
1 PAULO, mtumwi (wosacokera kwa anthu, kapena mwa munthu, koma mwa Yesu Kristu, ndi Mulungu Atate, amene anamuukitsa iye kwa akufa), 2 ndi abale onse amene ali pamodzi ndi ine,…
1 Pamenepo popita zaka khumi ndi zinai ndinakweranso kunka ku Yerusalemu pamodzi ndi Bamaba, ndinamtenganso Tito andiperekeze. 2 Koma ndinakwera kunkako mobvumbulutsa; ndipo ndinawauza Uthenga Wabwino umene ndiulalikira kwa amitundu;…
Cilamulo sicikhoza kupulumutsa; cititsogoiera kutifikitsa kwa Kristu 1 Agalatiya opusa inu, anakulodzani ndani, inu amene Kristu anaonetsedwa pa maso panu, wopacikidwa? 2 ici cokha ndifuna kuphunzira kwa inu, Kodi munalandira…
Uthenga Wabwino utimasula ku cilamulo 1 Koma ndinena kuti, pokhala wolowa nyumba ali wakhanda, sasiyana ndi kapolo, angakhale ali mwini zonse; 2 komatu ali wakumvera omsungira ndi adindo, kufikira nthawi…
Asunge ufulu wa Cikristu 1 Kristu anatisandutsa mfulu, kuti tikhale mfulu; cifukwa cace cirimikani, musakodwenso ndi gori la ukapolo. 2 Taonani, ine Paulo ndinena ndi inu, kuti, ngati mulola akuduleni,…
Malangizootsiriza; kulawirana 1 Abale, ngatinso munthu agwidwa nako kulakwa kwakuti, inu auzimu, mubweze wotereyo mu mzimu wa cifatso; ndikudzipenyerera wekha, ungayesedwe nawenso. 2 Nyamuliranani zothodwetsa, ndipo kotero mufitse cilamulo ca…
1 PAULO, mtumwi wa Kristu Yesu, mwa cifuniro ca Mulungu, kwa oyera mtima amene ali m’Efeso, ndi kwa iwo okhulupirika mwa Kristu Yesu: 2 Cisomo kwa inu, ndi mtendere wocokera…
Cipulumutso cicokera kucisomo 1 Ndipo inu, anakupatsani moyo, pokhala munali akufa ndi zolakwa, ndi zocimwa zanu, 2 zimene munayendamo kale, monga mwa mayendedwe a dziko lapansi lino, monga mwa mkulu…
Cinsinsi ca maitanidwe a amitundu 1 Cifukwa ca ici ine Paulo, ndine wandende wa Kristu Yesu cifukwa ca inu amitundu, 2 ngatitu munamva za udindo wa cisomo ca Mulungucimene anandipatsa…