Aroma 5

Zipatso za Cikhulupiriro 1 Popeza tsono tayesedwa olungama ndi cikhulupiriro, tikhala ndi mtendere ndi Mulungu mwa Ambuye wathu Yesu Kristu; 2 amene ife tikhoza kulowa naye ndi cikhulupiriro m’cisomo ici…

Aroma 6

Kristu anatityolera mphamvu ya zotpa 1 Cifukwa cace tidzatani? Tidzakhalabe m’ucimo kodi, kuti cisomo cicuruke? 2 Msatero ai. Ife amene tiri akufa ku ucimo, tidzakhala bwanji cikhalire m’menemo? 3 Kapena…

Aroma 7

Okhulupirira akwatiwa ndi Kristu 1 Nanga kodi simudziwa, abale, pakuti ndilankhula ndi anthu akudziwa lamulo, kuti lamulolo licita ufumu pa munthu nthawi zonse iye ali wamoyo? 2 Pakuti mkazi wokwatidwa…

Aroma 8

Mayo watha watsopano mwa Kristu 1 Cifukwa cace tsopano iwo akukhala mwa Kristu Yesu alibe kutsutsidwa. 2 Pakuti cilamulo ca mzimu wa moyo mwa Kristu Yesu candimasula ine ku lamulo…

Aroma 9

Paulo alirira kusamvera kwa Israyeli 1 Ndinena zoona mwa Kristu, sindinama ai, cikumbu mtima canga cicita umboni pamodzi ndine mwa Mzimu Woyera, 2 kuti ndagwidwa ndi cisoni cacikuru ndi kuphwetekwa…

Aroma 10

Ayuda anataya cilungamo ca Mulungu 1 Abale, kufunitsa kwa mtima wanga ndi pemphero langa limene ndiwapempherera kwa Mulungu, ndilo, kuti apulumuke. 2 Pakuti ndiwacitira iwo umboni kuti a ali ndi…

Aroma 11

Mulungu sanataya Aisrayeli onse 1 Cifukwa cace ndinena, Mulungu anataya anthu ace kodi? Msatero ai. Pakuti inenso ndiri M-israyeli, wa mbeu ya Abrahamu, wa pfuko la Benjamini. 2 Mulungu sanataya…

Aroma 12

Kudzipereka nsembe kwa Mulungu 1 Cifukwa cace ndikupemphani inu, abale, mwa zifundo za Mulungu, kuti mupereke matupi anu nsembe yamoyo, yopatulika, yokondweretsa, Mulungu, ndiko kupembedza kwanu koyenera. 2 Ndipo musafanizidwe…

Aroma 13

Kugonjera kwathu kwa akuru 1 Anthu onse amvere maulamuliro a akulu; pakuti palibe ulamuliro wina koma wocokera kwa Mulungu; ndipo iwo amene alipo aikidwa ndi Mulungu. 2 Kotero kuti iye…

Aroma 14

Cipiriro ca pa ofoka 1 Ndipo iye amene ali wofoka m’cikhulupiriro, mumlandire, koma si kucita naye makani otsutsana ai. 2 Munthu mmodzi akhulupirira kuti adye zinthu zonse, koma wina wofoka…