Macitidwe 23

1 Ndipo Paulo, popenyetsetsa a m’bwalo la akuru anati, Amuna, abale, ndakhala ine pamaso pa Mulungu ndi cikumbu mtima cokoma conse kufikira lero lomwe. 2 Ndipo mkulu wa ansembe Hananiya…

Macitidwe 24

Felike amva mlandu wa Paulo 1 Ndipo atapita masiku asanu anatsika mkulu wa ansembe Hananiya pamodzi ndi akuru ena, ndi wogwira moyo dzina lace Tertulo; ndipo anafotokozera kazembeyo za kunenera…

Macitidwe 25

Paulo pa bwalo la miranda la Festo. Anena akaturukira kwa Kaisara 1 Pamenepo Festo m’mene analowa dziko lace, ndipo atapita masiku atatu, anakwera kunka ku Yerusalemu kucokera ku Kaisareya. 2…

Macitidwe 26

1 Ndipo Agripa anati kwa Paulo, Kwaloleka udzinenere wekha. Pamenepo Paulo, anatambasula dzanja nadzikanira: 2 Ndidziyesera wamwai, Mfumu Agripa, popeza nditi ndidzikanira lero pamaso panu, za zonse zimene Ayuda andinenera…

Macitidwe 27

Amtumiza Paulo ku Roma. Tsoka panyanja 1 Ndipo pamene padatsimikizika kuti tipite m’ngalawa kunka ku Italiya, anapereka Paulo ndi andende ena kwa kenturiyo dzina lace Yuliyo, wa gulu la Augusto….

Macitidwe 28

Paulopa Melita 1 Ndipo titapulumuka, pamenepo tinadziwa kuti cisumbuco cinachedwa Melita. 2 Ndipo akunja anaticitira zokoma zosacitika pena ponsepo; pakuti anasonkha moto, natilandira ife tonse, cifukwa ca mvula inalinkugwa, ndi…

Aroma 1

1 PAULO, kapolowa Yesu Kristu, mtumwi woitanidwa, wopatulidwa kukanena Uthenga Wabwino wa Mulungu, 2 umene iye analonjeza kale ndi mau a ananeri ace m’malembo oyera, 3 wakunena za Mwana wace,…

Aroma 2

Kusamvera kwa Ayuda 1 Cifukwa cace uli wopanda mau owiringula, munthu iwe, amene uli yense wakuweruza; pakuti m’mene uweruza wina, momwemo udzitsutsa iwe wekha, pakuti iwe wakuweruza, umacita zomwezo. 2…

Aroma 3

Kuposa kwace kwa Myuda Mulungu ali wolungama 1 Ndipo potero Myuda aposa Dinji? Kapena mdulidwe upindulanji? 2 Zambiri monse monse: coyamba, kuti mau a Mulungu anaperekedwa kwa iwo. 3 Nanga…

Aroma 4

Abrahamu anayesedwa wolungama ndi cikhulupiriro 1 Ndipo tsono tidzanena kuti Abrahamu, kholo lathu monga mwa thupi, analandira ciani? 2 Pakuti ngati Abrahamu anayesedwa wolungama cifukwa ca nchito, iye akhala naco…