Macitidwe 13
Ulendo woyamba wa Paulo. Mpingo wa ku Antiokeya utuma Paulo ndi Bamaba amuke kwa amitundu, Alalikira pa Kupro, Elima watsenga 1 Ndipo kunali aneneri ndi aphunzioo ku Antiokeya mu Mpingo…
Ulendo woyamba wa Paulo. Mpingo wa ku Antiokeya utuma Paulo ndi Bamaba amuke kwa amitundu, Alalikira pa Kupro, Elima watsenga 1 Ndipo kunali aneneri ndi aphunzioo ku Antiokeya mu Mpingo…
Uthenga Wabwino ulalikidwa ku Ikoniyo, Lustra, ndi Derbe 1 Ndipo kunali pa Ikoniyo kuti analowa pamodzi m’sunagoge wa Ayuda, nalankhula kotero, kuti khamu lalikuru la Ayuda ndi Ahelene anakhulupira. 2…
Ku Yerusalemu atumwi ndi akuru aweruza za mdulidwe ndi malamulo a Mose 1 Ndipo anadza ena akutsika ku Yudeya, nawaphunzitsa abale, nati, Mukapandakudulidwa monga mwambo wa Mose, simungathe kupulumuka. 2…
1 Ndipo anafikanso ku Derbe ndi Lustra; ndipo taonani, panali wophunzira wina pamenepo, dzina lace Timoteo, amace ndiye Myuda wokhulupira; koma atate wace ndiye Mhelene. 2 Ameneyo anamcitira umboni wabwino…
Paulo ku Tesalonika ndi Bereya 1 Pamene anapitirira pa Amfipoli, ndi Apoloniya, anafika ku Tesalonika, kumene kunali sunagoge wa Ayuda. 2 Ndipo Paulo, monga amacita, analowa kwa iwo; ndipo masabata…
Paulo ku Korinto ndi ku Efeso, Abwera ku Yerusalemu 1 Zitapita izi anacoka ku Atene, nadza ku Korinto. 2 Ndipo anapeza Myuda wina dzina lace Akula, pfuko lace la ku…
Ulendo wacitatu wa Paulo. Demetrio autsa phokoso 1 Ndipo panali, pamene Apolo anali ku Korinto, Paulo anapita pa maiko a pamtunda, nafika ku Efeso, napeza akuphunzira ena; 2 ndipo anati…
Paulo apitanso ku Makedoniya; ndi Helene, ndi Asiya 1 Ndipo litaleka phokoso, Paulo anaitana ophunzirawo, ndipo m’mene anawacenjeza, analawirana nao, naturuka kunka ku Makedoniya. 2 Ndipo m’mene atapitapita m’mbali zijazo,…
Paulo atabwera, ku Yerusalemu amgwira m’Kacisi 1 Ndipo kunali, titalekana nao ndi kukankha ngalawa, tinadza molunjika ku Ko, ndi m’mawa mwace ku Rode, ndipo pocokerapo ku Patara; 2 ndipo m’mene…
Paulo acita codzikanira cace kwa anthu 1 Amuna, abale, ndi atate, mverani codzikanira canga tsopano, ca kwa inu. 2 Ndipo pakumva kuti analankhula nao m’cinenedwe ca Cihebri, anaposa kukhala cete;…