Macitidwe 3

Wopunduka cibadwire aciritsidwa. Conenera Petro m’Kacisi 1 Koma Petro ndi Yohane analikukwera kunka kuKacisi pa ora lakupembedza, ndilo lacisanu ndi cinai. 2 Ndipo munthu wina wopunduka miyendo cibadwire ananyamulidwa, amene…

Macitidwe 4

Petro ndi Yohane ku bwalo la akuru 1 Koma m’mene analikulankhula ndi anthu, ansembe ndi mdindo wa kuKacisi ndi Asaduki anadzako, 2 obvutika mtima cifukwa anaphunzitsa anthuwo, nalalikira mwa Yesu…

Macitidwe 5

Za Hananiya ndi Safira 1 Koma munthu wina dzina lace Hananiya pamodzi ndi Safira mkazi wace, 2 anagulitsa cao, napatula pa mtengo wace, mkazi yemwe anadziwa, natenga cotsala, naciika pa…

Macitidwe 6

Asankha atumiki asanu ndi awiri 1 Koma masiku awo, pakucurukitsa ophunzira, kunauka cidandaulo, Aheleniste kudandaula pa Ahebri, popeza amasiye ao anaiwalika pa citumikiro ca tsiku ndi tsiku. 2 Ndipo khumi…

Macitidwe 7

1 Ndipo mkulu wa ansembe anati, Zitero izi kodi? 2 Ndipo Stefano anati, Amuna inu, abale, ndi atate, tamverani. Mulungu wa ulemerero anaonekera kwa kholo lathu Abrahamu, pokhala iye m’Mesopotamiya,…

Macitidwe 8

Uthenga Wabwino pa Samariya. Simoni wanyanga 1 Ndipo Saulo analikubvomerezana nao pa imfa yace. Ndipo tsikulo kunayamba kuzunza kwakukuru pa Mpingo unali m’Yerusalemu; ndipo anabalalitsidwa onse m’maiko a Yudeya ndi…

Macitidwe 9

Kusandulika mtima kwa Paulo pa njira ya ku Damasiko 1 Koma Saulo, wosaleka kupumira pa akuphunzira a Ambuye kuopsya ndi kupha, ananka kwa mkulu wa ansembe, 2 napempha kwa iye…

Macitidwe 10

Kenturiyo Komeliyo 1 Ndipo kunali munthu ku Kaisareya, dzina lace Komeliyo, kenturiyo wa gulu lochedwa la Italiya, 2 ndiye munthu wopembedza, ndi wakuopa Mulungu ndi banja lace lonse, amene anapatsa…

Macitidwe 11

Petro adziwerengera pamaso pa Mpingo kuti anabatiza Komeliyo 1 Koma atumwi ndi abale akukhala m’Yudeya anamva kuti amitundunso adalandira mau a Mulungu. 2 Ndipo pamene Petro adakwera kudza ku Yerusalemu,…

Macitidwe 12

Herode azunza Eklesia; amupha Yakobo, naponya Petro kundende. Petro apulumuka m’ndende. Imfa ya Herode 1 Koma nyengo imeneyo Herode mfumu anathira manja ena a m’Eklesia kuwacitira zoipa. 2 Ndipo adapha…