Yohane 14
Yesu aneneratu za kubweranso kwace 1 Mtima wanu usabvutike; mukhulupirira Mulungu, khulupirirani Inenso. 2 M’nyumba ya Atate wanga alimo malo okhalamo ambiri. Ngati sikudali kutero, ndikadakuuzani inu; pakuti ndipita kukukonzerani…
Yesu aneneratu za kubweranso kwace 1 Mtima wanu usabvutike; mukhulupirira Mulungu, khulupirirani Inenso. 2 M’nyumba ya Atate wanga alimo malo okhalamo ambiri. Ngati sikudali kutero, ndikadakuuzani inu; pakuti ndipita kukukonzerani…
Mpesa ndi nthambi zace 1 Ine ndine mpesa weniweni, ndipo Atate wanga ndiye wam’munda. 2 Nthambi iri yonse ya mwa Ine yosabala cipatso, aicotsa; ndi iri y’onse yakubala cipatso, aisadza,…
Awacenjeza za kuzunzidwa 1 Izi ndalankhula ndi inu kuti mungakhumudwitsidwe. 2 Adzakuturutsani m’masunagoge; koma ikudza nthawi imene yense wakupha inu adzayesa kuti atumikira Mulungu, 3 Ndipo izi adzacita, cifukwa sanadziwa…
Yesu apempherera akuphunzira ace 1 Zinthu izi analankhula Yesu; ndipo m’mene anakweza maso ace Kumwamba, anati, Atate, yafika nthawi; lemekezani Mwana wanu, kuti Mwana wanu akulemekezeoi Inu; 2 monga mwampatsa…
Yesu m’Getsemane 1 M’mene Yesu adanena izi, anaturuka ndi akuphunzira ace, kunka tsidya lija la mtsinje wa Kedroni, kumene kunali munda, umene analowamo iye ndi akuphunzira ace. Aperekedwa namangidwa 2…
1 Pamenepo tsono Pilato anatenga Yesu, namkwapula. 2 Ndipo asilikari, m’mene analuka korona waminga anambveka pamutu pace, nampfunda iye maraya acibakuwa; 3 nadza kwa iye, nanena, Tikuoneni, Mfumu ya Ayuda!…
Yesu auka kwa akufa 1 Koma tsiku loyamba la Sabata anadza Mariya wa Magadala mamawa, kusanayambe kuca, kumanda, napenya mwala wocotsedwa kumanda. 2 Pomwepo anathamanga nadza kwa Simoni Petro ndi…
Yesu awaonekera ku nyanja ya Tiberiva 1 Zitapita izi Yesu anadzionetseranso kwa akuphunzira ace ku nyanja ya Tiberiya. Koma anadzionetsera cotere. 2 Anali pamodzi Simoni Petro, ndi Tomasi, wochedwa Didimo,…
Yesu akwera kunka Kumwamba 1 TAONANI Teofilo inu, mau aja oyamba ndinakonza, za zonse Yesu anayamba kuzicita ndi kuziphunzitsa, 2 kufikira tsiku lija anatengedwa kunka Kumwamba, atatha kulamulira mwa Mzimu…
Tsiku la Pentekoste 1 Ndipo pakufika tsiku la Penteskoste, anali onse pamodzi pa malo amodzi. 2 Ndipo mwadzidzidzi anamveka mau ocokera Kumwamba ngati mkokomo wa mphepo yolimba, nadzaza nyumba yonse…