Yohane 4
Mkazi wa ku Samariya 1 Cifukwa cace pamene Ambuye anadziwa kuti Afarisi adamva kuti Yesu anayesa anthu ophunzira, nawabatiza koposa Yohane 2 (angakhale Yesu sanabatiza yekha koma ophunzira ace), 3…
Mkazi wa ku Samariya 1 Cifukwa cace pamene Ambuye anadziwa kuti Afarisi adamva kuti Yesu anayesa anthu ophunzira, nawabatiza koposa Yohane 2 (angakhale Yesu sanabatiza yekha koma ophunzira ace), 3…
Yesu aciritsa wopuwala ku thamanda La Betesda 1 Zitapita izi panali phwando la Ayuda; ndipo Yesu anakwera kunka ku Yerusalemu. 2 Koma pali thamanda m’Yerusalemu pa cipata ca nkhosa, lochedwa…
Yesu acurukitsa mikate 1 Zitapita izi anacoka Yesu kunka ku tsidya lija la nyanja ya Galileya, ndiyo ya Tiberiya, 2 Ndipo khamu lalikuru la anthu linamtsata iye, cifukwa anaona zizindikilo…
Abale a Yesu sambvomereza 1 Ndipo zitapita izi Yesu anayendayenda m’Galileya; pakuti sanafuna kuyendayenda m’Yudeya, cifukwa Ayuda anafuna kumupha iye. 2 Koma phwando la Ayuda, phwando la misasa, linayandikira. 3…
Za mkazi wacigololo 1 Koma Yesu anamuka ku phiri la Azitona. 2 Komac mamawa anadzanso kuKacisi, ndipo anthu onse anadza kwa iye; ndipo m’mene anakhala pansi anawaphunzitsa. 3 Koma alembi…
Aciritsidwa munthu wosaona cibadwire 1 Ndipo popita, anaona munthu ali wosaona cibadwire. 2 Ndipo akuphunzira ace anamfunsa iye, nanena, Rabi, anacimwa ndani, ameneyo, kapena atate wace ndi amace, kuti anabadwa…
Za Mbusa Wabwino 1 Indetu, indetu, ndinena ndi inu, Iye wosalowa m’khola la nkhosa pakhomo, koma akwerera kwina, iyeyu ndiye wakuba ndi wolanda. 2 Koma iye wakulowera pakhomo, ndiye mbusa…
Ciukitso ca Lazaro 1 Koma panali munthu wodwala, Lazaro wa ku Betaniya, wa m’mudzi wa Mariya ndi mbale wace Marita. 2 Koma ndiye Mariya uja anadzoza Ambuye ndi mafuta onunkhira…
Mariya adzoza mapazi a Yesu 1 Pomwepo anatsala masiku asanu ndi limodzi asanafike Paskha, Yesu anadza ku Betaniya kumene kunali Lazaro, amene Yesu adamuukitsa kwa akufa. 2 Ndipo anamkonzera iye…
Yesu asambitsa mapazi a anyamata ace 1 Koma pasanafike phwando la Paskha, Yesu, podziwa kuti nthawi yace idadza yakucoka kuturuka m’dziko lino lapansi, kunka kwa Atate, m’mene anakonda ace a…