Luka 18

Fanizo la woweruza wosalungama 1 Ndipo anawanenera fanizo lakuti ayenera iwo kupemphera nthawi zonse, osafoka mtima; 2 nanena, M’mudzi mwakuti munali woweruza wosaopa Mulungu, ndi wosasamala munthu. 3 Ndipo m’mudzimo…

Luka 19

Zakeyu asandulika mtima 1 Ndipo analowa, napyola pa Yeriko. Ndipo taonani, mwamuna wochedwa dzina lace Zakeyu; 2 ndipo Iye anali mkulu wa amisonkho, nali wacuma. 3 Ndipo anafuna kuona Yesu…

Luka 20

Amfunsa Yesu za ulamuliro wace 1 Ndipo kunali lina la masiku awo m’mene iye analikuphunzitsa anthu m’Kacisi, ndi kulalikira Uthenga Wabwino, adamdzera ansembe akulu ndi alembi pamodzi ndi akulu; 2…

Luka 21

Mphatso ya mkazi wamasiye 1 Ndipo Yesu anakweza maso, naona anthu eni cuma alikuika zopereka zao mosungiramo ndalama. 2 Ndipo anaona mkazi wina wamasiye waumphawi alikuika momwemo timakobiri tiwiri. 3…

Luka 22

Yudase apangana kupereka Yesu 1 Ndipo phwando la mikate yopanda cotupitsa linayandikira, ndilo lochedwa Paskha. 2 Ndipo ansembe akuru ndi alembi anafunafuna maphedwe ace pakuti anaopa anthuwoo. 3 Ndipo Satana…

Luka 23

Yesu na bwalo la Pilato 1 Ndipo khamu lonselo Iinanyamuka kupita naye kwa Pilato. 2 Ndipo anayamba kumnenera iye, kuti, Tinapeza munthu uyu alikupandutsa anthu a mtundu wathu, ndi kuwaletsa…

Luka 24

Yesu auka kwa akufa 1 Koma tsiku loyamba la sabata, mbanda kuca, anadza kumanda atatenga zonunkhira adazikonza. 2 Ndipo anapeza mwala unakunkhunizidwa kuucotsa pamanda. 3 Ndipo m’mene analowa sanapeza mtembo…

Yohane 1

Umulungu wa Yesu Kristu 1 PACIYAMBI panali Mau, ndipo Mau anali kwa Mulungu, ndipo Mau ndiye Mulungu. 2 Awa anali paciyambi kwa Mulungu, 3 Zonse: zinalengedwa ndi iye; ndipo kopanda…

Yohane 2

Yesu asandutsa madzi vinyo ku Kana 1 Ndipo tsiku lacitatu pariali ukwati m’Kana wa m’Galileya; ndipo amace wa Yesu anali komweko. 2 Ndipo Yesu yemwe ndi akuphunzira ace anaitanidwa ku…

Yohane 3

Yesu aphunzitsa Nikodemo za kubadwa kwatsopano 1 Koma panali munthu wa Afarisi, dzina lace Nikodemo, mkulu wa Ayuda, 2 Iyeyu anadza kwa Yesu usiku, nati kwa iye, Rabi, tidziwa kuti…