Levitiko 1
Za nsembe yopsereza 1 NDIPO Yehova anaitana Mose, nanena naye ali m’cihema cokomanako iye, nati, 2 Lankhula ndi ana a lsrayeli, nunene nao, Ali yense mwa inu akabwera naco copereka…
Za nsembe yopsereza 1 NDIPO Yehova anaitana Mose, nanena naye ali m’cihema cokomanako iye, nati, 2 Lankhula ndi ana a lsrayeli, nunene nao, Ali yense mwa inu akabwera naco copereka…
Za nsembe yaufa ndi ya zipatso zoyamba 1 Ndipo munthu akabwera naco copereka ndico nsembe yaufa ya kwa Yehova, copereka cace cizikhala ca ufa wosalala; ndipo athirepo mafuta, ndi kuikapo…
Za nsembe yoyamika 1 Ndipo copereka cace cikakhala nsembe yoyamika; akabwera nayo ng’ombe, kapena yaimuna kapena yaikazi, azibwera nayo yopanda cirema pamaso pa Yehova. 2 Ndipo aike dzanja lace pa…
Za nsembe yaucimo pocimwa wansembe 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Lankhula ndi ana a Israyeli, ndi kuti, Munthu akacimwa, osati dala, pa cina ca zinthu ziri zonse…
Za nsembe yoparamula 1 Ndipo akacimwa munthu, wakuti adamva mau akuwalumbiritsa, ndiye mboni, kapena wakuona, kapena wakudziwa, koma osaulula, azisenza mphulupulu yace; 2 kapena munthu akakhudza ciri conse codetsa kapena…
Za nsembe yoparamula pocimwa dala munthu 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, ndi kuti, 2 Akacimwa munthu nakacita mosakhulupirika pa Yehova nakacita monyenga ndi mnansi wace kunenaza coikiza, kapena cikole,…
Cilamulo ca nsembe yo paramula 1 Ndipo cilamulo ca nsembe yoparamula ndi ici: ndiyo yopatulikitsa. 2 Pamalo pophera nsembe yopsereza ndipo aziphera nsembe yoparamula; nawaze mwazi wace pa guwa la…
Kupatulidwa kwa ansembe 1 Ndipo Yehova ananena ndi Mose, nati, 2 Tenga Aroni ndi ana ace pamodzi naye ndi zobvalazo, ndi mafuta odzozawo, ndi ng’ombe ya nsembe yaucimoyo, ndi nkhosa…
Aroni adziperekera yekha ndi anthu nsembe, ndizo nsembe zoyamba 1 Ndipo kunali, tsiku lacisanu ndi citatu, kuti Mose anaitana Aroni ndi ana ace amuna, ndi akuru a Israyeli; 2 ndipo…
Kucimwa ndi kuphedwa kwa Nadabu ndi Abihu 1 Ndipo ana a Aroni, Nadabu ndi Abihu anatenga yense mbale yace ya zofukiza, naikamo moto, naikapo cofukiza, nabwera nao pamaso pa Yehova…