Yoweli 1

Tsoka locokera ku dzombe ndi cirala 1 MAU a Yehova a kwa Yoeli mwana wa Petueli. 2 Imvani ici, akulu akulu inu, nimuchere khutu, inu nonse okhala m’dziko. Cacitika ici…

Yoweli 2

Cilango coopsa ca Mulungu 1 Muombe lipenga m’Ziyoni, nimupfuulitse m’phiri langa lopatulika; onse okhala m’dziko anjenjemere; pakuti tsiku la Yehova lirinkudza, pakuti liyandikira; 2 tsiku la mdima, la mdima wandiweyani,…

Yoweli 3

Aneneratu za cilango ca Mulungu pa adani ace; Israyeli adzakonrekanso 1 Pakuti taonani, masiku awo, ndi nthawi iyo, pamene ndibwera nao andende a Yuda ndi a Yerusalemu, 2 ndidzasonkhanitsa amitundu…