Yoswa 21

Midzi yokhalamo Alevi 1 Pamenepo akuru a nyumba za atate a Alevi anayandikira kwa Eleazare wansembe, ndi kwa Yoswa mwana wa Nuni, ndi kwa akuru a nyumba za atate a…

Yoswa 22

A pfuko la Rubeni, la Gadi, ndi la Manase logawika pakati, amuka kwao kum’mawa kwa Yordano 1 Pamenepo Yoswa anaitana Arubeni ndi Agadi, ndi pfuko la Manase logawika pakati, 2…

Yoswa 23

Yoswa acenjeza anthu asunge Malamulo a Mulungu 1 Ndipo atapita masiku ambiri, Yehova atapumulitsa Israyeli kwa adani ao onse akuwazungulira, ndipo Yoswa adakalamba nakhala wa zaka zambiri; 2 Yoswa anaitana…

Yoswa 24

Yoswa akumbutsa anthu zowacitira Mulungu 1 Ndipo Yoswa anasonkhanitsa mapfuko onse a Israyeli ku Sekemu, naitana akulu akulu a Israyeli ndi akuru ao, ndi oweruza ao, ndi akapitao ao; ndipo…