Yoswa 11

Yoswa agonjetsa mafumu a kumpoto 1 Ndipo kunali, pamene Yabini mfumu ya ku Hazoro anacimva, anatwna kwa Yabobu mfumu ya ku Madoni, ndi kwa mfumu ya ku Simironi, ndi kwa…

Yoswa 12

Mafumu amene ana a Israyeli anawakantha 1 Ndipo awa ndi mafumu a dzikolo amene ana a Israyeli anwakantha, nalanda dziko lao tsidya la Yordano kum’mawa, kuyambira cigwa ca Arimoni, mpaka…

Yoswa 13

Cigawo ca dziko la kum’mawa kwa Yordano 1 Ndipo Yoswa anakalamba, wa zaka zambiri; ndipo Yehova ananena naye, Wakalamba, wa zaka zambiri, ndipo latsala dziko lalikurukuru, alilandire colowa cao, 2…

Yoswa 14

Kalebe alandira Hebroni 1 Ndipo awa ndi maiko ana a Israyeli anawalanda m’dziko la Kanani, amene Eleazare wansembe, ndi Yoswa mwana wa Nuni, ndi akulu a nyumba za atate a…

Yoswa 15

Malire a Yuda 1 Ndipo gawo la pfuko la ana a Yuda monga mwa mabanja ao linafikira malire a Edomu, ku cipululu ca Zini kumwera, ku malekezero a kumwera. 2…

Yoswa 16

Malire a Efraimu 1 Ndipo gawo La ana a Yosefe linaturuka kucokera ku Yordano ku Yeriko, ku madzi a Yeriko kum’mawa, kucipululu, nakwera kucokera ku Yeriko kumka kumapiri ku Beteli;…

Yoswa 17

Malire a Manase 1 Gawo la pfuko la Manase ndi ili: pakuti anali woyamba wa Yosefe. Makiri mwana woyamba wa Manase, atate wa Gileadi, popeza ndiye munthu wa nkhondo, anakhala…

Yoswa 18

Autsa cihema ku Silo 1 Ndipo msonkhano wonse wa ana a Israyeli unasonkhana ku Silo, nuutsa komweko cihema cokomanako; ndipo dziko linawagoniera. 2 Ndipo anatsala mwa ana a Israyeli mapfuko…

Yoswa 19

Malire a Simeoni 1 Ndipo maere aciwiri anamturukira Simeoni, pfuko la ana a Simeoni monga mwa mabanja ao; ndi colowa cao cinali pakati pa colowa ca ana a Yuda. 2…

Yoswa 20

Midzi yopulumukirako 1 Ndipo Yehova anati kwa Yoswa, 2 Nena ndi ana a Israyeli ndi kuti, Mudziikire midzi yopulumukirako, monga ndinanena kwa inu mwa dzanja la Mose, 3 kuti athawireko…