Yoswa 1
1 NDIPO atafa Mose mtumiki wa Yehova, Yehova anati kwa Yoswa mwana wa Nuni mnyamata wa Mose, 2 Mose mtumiki wanga wafa; tauka tsono, nuoloke Yordano uyu, iwe ndi anthu…
1 NDIPO atafa Mose mtumiki wa Yehova, Yehova anati kwa Yoswa mwana wa Nuni mnyamata wa Mose, 2 Mose mtumiki wanga wafa; tauka tsono, nuoloke Yordano uyu, iwe ndi anthu…
Yoswa atuma anthu awiri azonde Yeriko 1 Ndipo Yoswa mwana wa Nuni, ali ku Sitimu, anatuma amuna awiri mosadziwika kukazonda, ndi kuti, Mukani, mulipenye dzikolo, ndi ku Yeriko. Ndipo anamuka…
Aisrayeli aoloka Yordano 1 Ndipo Yoswa analawirira mamawa, kucoka ku Sitimu, nafika ku Yordano, iye ndi ana onse a Israyeli; nagona komweko, asanaoloke. 2 Ndipo kunali atapita masiku atatu, akapitao…
Aimiritsa miyala 12 ikhale cikumbutso ku Giligala 1 Ndipo kunali, utatha kuoloka Yordano mtundu wonse, Yehova ananena ndi Yoswa, nati, 2 Mudzitengere mwa anthu, amuna khumi ndi awiri, pfuko limodzi…
Anthu adulidwa nacita Paskha 1 Ndipo kunali, pamene mafumu onse a Aamori okhala tsidya la kumadzulo la Yordano, ndi mafumu onse a Akanani okhala ku Nyanja ya Mcere anamvakuti Yehova…
Kupasulidwa kwa Yeriko 1 Koma ku Yeriko anatseka pazipata, natsekedwa cifukwa ca ana a Israyeli, panalibe woturuka, panalibenso wolowa. 2 Ndipo Yehova ananena kwa Yoswa, Taona, ndapereka m’dzanja lako Yeriko…
Kucimwa kwa Akani 1 Koma ana a Israyeli analakwa ndi coperekedwaco; popeza Akani mwana wa Karimi, mwana wa Zabidi, mwana wa Zera, wa pfuko la Yuda, anatapa coperekedwaco; ndi mkwiyo…
Kupasulidwa kwa Ai 1 Pamenepo Yehova anati kwa Yoswa, Usaope, kapena kutenga nkhawa, tenga anthu onse a nkhondo apite nawe, ndipo tauka, kwera ku Ai; taona, ndapereka m’dzanja lako mfumu…
1 Yoswa anyengedwa ndi Agibeoni napangana nao. Ndipo kunali, pakumva ici mafumu onse a tsidya ilo la Yordano, kumapiri ndi kucidikha, ndi ku madoko onse a nyanja yaikuru, pandunji pa…
Cinkhondo ku Gibeoni 1 Ndipo kunali, pamene Adoni-Zedeki mfumu ya Yerusalemu anamva kuti Yoswa adalanda Ai, ndi kumuononga konse; nacitira Ai ndi mfumu yace monga adacitira Yeriko ndi mfumu yace;…