Yona 1
Kuitanidwa kwa Yona, kuthawa kwace, ndi kulangidwa kwace 1 NDIPO mau a Yehova anadza kwa Yona mwana wa Amitai, ndi kuti, 2 Nyamuka, pita ku Nineve, mudzi waukuruwo, nulalikire motsutsana…
Kuitanidwa kwa Yona, kuthawa kwace, ndi kulangidwa kwace 1 NDIPO mau a Yehova anadza kwa Yona mwana wa Amitai, ndi kuti, 2 Nyamuka, pita ku Nineve, mudzi waukuruwo, nulalikire motsutsana…
Pemphero la Yona ali m’mimba mwa cinsomba 1 Pamenepo Yona anapemphera kwa Yehova Mulungu wace ali m’mimba mwa nsombayo. 2 Ndipo anati, Ndinaitana Yehova m’nsautso yanga, Ndipo anandiyankha ine; Ndinapfuula…
Yona ku Nineve, Kulapa kwa a ku Nineve 1 Ndipo mau a Yehova anadza kwa Yona nthawi yaciwiri, ndi kuti, 2 Nyamuka, pita ku Nineve mudzi waukuru uja, nuulalikire uthenga…
Kudandaula kwa Yona, kumdzudzula kwa Mulungu 1 Koma sikudakomera Yona konse, ndipo anapsa mtima. 2 Ndipo anapemphera kwa Yehova, nati, Ha, Yehova! si ndiwo mau anga ndikali m’dziko langa? cifukwa…