Yohane 21

Yesu awaonekera ku nyanja ya Tiberiva 1 Zitapita izi Yesu anadzionetseranso kwa akuphunzira ace ku nyanja ya Tiberiya. Koma anadzionetsera cotere. 2 Anali pamodzi Simoni Petro, ndi Tomasi, wochedwa Didimo,…