Yohane 1
Umulungu wa Yesu Kristu 1 PACIYAMBI panali Mau, ndipo Mau anali kwa Mulungu, ndipo Mau ndiye Mulungu. 2 Awa anali paciyambi kwa Mulungu, 3 Zonse: zinalengedwa ndi iye; ndipo kopanda…
Umulungu wa Yesu Kristu 1 PACIYAMBI panali Mau, ndipo Mau anali kwa Mulungu, ndipo Mau ndiye Mulungu. 2 Awa anali paciyambi kwa Mulungu, 3 Zonse: zinalengedwa ndi iye; ndipo kopanda…
Yesu asandutsa madzi vinyo ku Kana 1 Ndipo tsiku lacitatu pariali ukwati m’Kana wa m’Galileya; ndipo amace wa Yesu anali komweko. 2 Ndipo Yesu yemwe ndi akuphunzira ace anaitanidwa ku…
Yesu aphunzitsa Nikodemo za kubadwa kwatsopano 1 Koma panali munthu wa Afarisi, dzina lace Nikodemo, mkulu wa Ayuda, 2 Iyeyu anadza kwa Yesu usiku, nati kwa iye, Rabi, tidziwa kuti…
Mkazi wa ku Samariya 1 Cifukwa cace pamene Ambuye anadziwa kuti Afarisi adamva kuti Yesu anayesa anthu ophunzira, nawabatiza koposa Yohane 2 (angakhale Yesu sanabatiza yekha koma ophunzira ace), 3…
Yesu aciritsa wopuwala ku thamanda La Betesda 1 Zitapita izi panali phwando la Ayuda; ndipo Yesu anakwera kunka ku Yerusalemu. 2 Koma pali thamanda m’Yerusalemu pa cipata ca nkhosa, lochedwa…
Yesu acurukitsa mikate 1 Zitapita izi anacoka Yesu kunka ku tsidya lija la nyanja ya Galileya, ndiyo ya Tiberiya, 2 Ndipo khamu lalikuru la anthu linamtsata iye, cifukwa anaona zizindikilo…
Abale a Yesu sambvomereza 1 Ndipo zitapita izi Yesu anayendayenda m’Galileya; pakuti sanafuna kuyendayenda m’Yudeya, cifukwa Ayuda anafuna kumupha iye. 2 Koma phwando la Ayuda, phwando la misasa, linayandikira. 3…
Za mkazi wacigololo 1 Koma Yesu anamuka ku phiri la Azitona. 2 Komac mamawa anadzanso kuKacisi, ndipo anthu onse anadza kwa iye; ndipo m’mene anakhala pansi anawaphunzitsa. 3 Koma alembi…
Aciritsidwa munthu wosaona cibadwire 1 Ndipo popita, anaona munthu ali wosaona cibadwire. 2 Ndipo akuphunzira ace anamfunsa iye, nanena, Rabi, anacimwa ndani, ameneyo, kapena atate wace ndi amace, kuti anabadwa…
Za Mbusa Wabwino 1 Indetu, indetu, ndinena ndi inu, Iye wosalowa m’khola la nkhosa pakhomo, koma akwerera kwina, iyeyu ndiye wakuba ndi wolanda. 2 Koma iye wakulowera pakhomo, ndiye mbusa…