Yobu 41
1 Kodi ukhoza kukoka ng’ona ndi mbedza? Kapena kukanikiza kalandira wace ndi cingwe? 2 Kodi ukhoza kumanga m’mphuno ndi mlulu? Kapena kuboola nsagwada wace ndi momba? 3 Kodi idzacurukitsa mau…

Yobu adzicepetsa pamaso pa Mulungu, mabwenziwo adzudzulidwa ndi Mulungu, Yobu apulumutsidwa nadalitsidwanso 1 Pamenepo Yobu anayankha Mulungu, nati, 2 Ndidziwa kuti mukhoza kucita zonse, Ndi kuti palibe coletsa colingirira canu…