Yobu 31
1 Ndinapangana ndi maso anga, Potero ndipenyerenji namwali? 2 Pakuti gawo la Mulungu locokera kumwamba, Ndi colowa ca Wamphamvuyonse cocokera m’mwambamo nciani? 3 Si ndizo cionongeko ca wosalungama, Ndi tsoka…
1 Ndinapangana ndi maso anga, Potero ndipenyerenji namwali? 2 Pakuti gawo la Mulungu locokera kumwamba, Ndi colowa ca Wamphamvuyonse cocokera m’mwambamo nciani? 3 Si ndizo cionongeko ca wosalungama, Ndi tsoka…
Elihu adzudzula Yobu ndi mabwenzi atatu omwe 1 Pamenepo amuna atatuwa analeka kumyankha Yobu; pakuti anali wolungama pamaso pace pa iye mwini. 2 Ndipo adapsa mtima Elihu mwana wa Barakeli…
Elihu atsutsa Yobu pa kudzikuza kwace, nanenetsa kuti pomlanga munthu Mulungu ali naco cifukwa 1 Komatu, Yobu, mumvere maneno anga, Mucherere khutu mau anga. 2 Taonani tsono, ndatsegula pakamwa panga,…
Elihu anenetsa Mulungu sangathe kukhala wosalungama, koma asiyanitsa pakati pa okoma ndi oipa 1 Ndipo Elihu anabwereza kunena, nati, 2 Tamverani mau anga, inu anzeru; Mundicherere khutu inu akudziwa. 3…
Elihu akuti kwa Mulungu kulibe cifukwa ca kucita tsankhu 1 Ndipo Elihu anabwereza kunena, nati, 2 Kodi muciyesa coyenera, Umo mukuti, Cilungamo canga ciposa ca Mulungu, 3 Pakuti munena, Upindulanji…
Elihu alemekeza cilungamo ndi mphamvu ya Mulungu. Mulungu ndi wangwiro, ife tilephera kumdziwa 1 Elihu nabwereza, nati, 2 Mundilole pang’ono, ndidzakuuzani, Pakuti ndiri naonso mau akunenera Mulungu. 3 Ndidzatenga nzeru…
1 Pa icinso mtima wanga unienjemera, Nusunthika m’malo mwace. 2 Mvetsetsani cibumo ca mau ace, Ndi kugunda koturuka m’kamwa mwace. 3 Akumveketsa pansi pa thambo ponse, Nang’anipitsa mphezi yace ku…
Mulungu aonekera kwa Yobu osamtsutsa. Koma amkumbutsa za ukuru wopambana wa Mulungu. Yobu adzicepetsapo 1 Pamenepo Yehova anayankha Yobu m’kabvumvulu, nati, 2 Ndani uyu adetsa uphungu, Ndi mau opanda nzeru?…
1 Kodi udziwa nyengo yakuswana zinkhoma? Kodi wapenyerera pakuswa nswala? 2 Ukhoza kodi kuwerenga miyezi yakuzipitira, Kapena udziwa nyengo yoti ziswane? 3 Zithuntha, ziswa, Zitaya zowawa zao. 4 Ana ao…
1 Ndipo Yehova anabwereza kwa Yobu, nati, 2 Kodi wodzudzulayo atsutsane ndi Wamphamvuyonse? Wocita makani ndi Mulungu ayankhe. 3 Pamenepo Yobu anayankha Yehova, nati, 4 Taonani, ndakhululuka ine, ndidzakubwezerani mau…