Yobu 21

Yobu ayankha kuti oipa ambiri amalemerera. Zooneka m’maso sizitiuza za mtima wa Mulungu 1 Pamenepo Yobu anayankha, nati, 2 Mvetsetsani mau anga; Ndi ici cikhale citonthozo canu. 3 Mundilole, ndinene…

Yobu 22

Elifazi amchulira Yobu zoipa zambiri, namuuza alape, Mulungu nadzamcitira cifundo 1 Pamenepo Elifazi wa ku Temani anayankha, nati, 2 Kodi munthu apindulira Mulungu? Koma wanzeru angodzipindulira yekha. 3 Kodi Wamphamvuyonse…

Yobu 23

Yobu abwereza kukana kuti sanacimwa. Mulungu wosadziwika acita cifuniro cace. Kwambiri ocimwa oyenera kulangidwa akhala bwino m’moyo uno 1 Koma Yobu anayankha, nati, 2 Lero lomwe kudandaula kwanga kumawawa; Kulanga…

Yobu 24

1 Wamphamvuyonse alekeranji kuikiratu nyengo? Ndi iwo omdziwa alekeranji kudziwa masiku ace? 2 Alipo akusendeza malire; Alanda gulu la zoweta, nazidyetsa. 3 Akankhizira kwao buru wa amasiye, Atenga ng’ombe ya…

Yobu 25

Bilidadi akuti munthu sayenera kudziyesa wolungama pamaso pa Mulungu 1 Pamenepo Bilidadi wa ku Suki anayankha, nati, 2 Kulamulira ndi kuopsa kuti ndi Iye; Acita mtendere pa zam’mwamba zace. 3…

Yobu 26

Yobu atsutsa Bilidadi kuti sanamthandiza; yekha nalemekeza ukulu wa Mulungu 1 Koma Yobu anayankha, nati, 2 Wamthandiza bwanji wopanda mphamvu, Kulipulumutsa dzanja losalimba! 3 Wampangira bwanji wopanda nzeruyu! Ndi kudziwitsa…

Yobu 27

Yobu adzikaniza nanenetsa kuti ocimwa ambiri akhala osalangidwa. Ena ali ndi nzeru ndi cuma, koma opanda nzeru yeni yeni 1 Ndipo Yobu anaonjezanso mwambi wace, nati, 2 Pali Mulungu, amene…

Yobu 28

1 Koma kuli mtapo wa siliva, Ndi malo a golidi amene amuyenga. 2 Citsulo acitenga m’nthaka, Ndi mkuwa ausungunula kumwala. 3 Munthu athawitsa mdima, Nafunafuna mpaka malekezero onse, Miyala ya…

Yobu 29

Yobu alinganiza cikhalidwe cace cakale ndi tsoka latsopano, nalimbika kuti sanacita zochulidwazi 1 Ndipo Yobu anaonjezanso mwambi wace, nati, 2 Ha! ndikadakhala monga m’miyezi yapitayi, Monga m’masiku akundisunga Mulungu; 3…

Yobu 30

1 Koma tsopano iwo osafikana msinkhu wanga andiseka, Iwo amene atate ao ndikadawapeputsa, osawaika pamodzi ndi agaru olinda nkhosa zanga. 2 Mphamvunso ya m’manja mwao ndikadapindulanji nayo? Ndiwo anthu amene…