Yobu 1

Yobu wosautsidwabe alimbika kutama Mulungu 1 PANALI munthu m’dziko la Uzi, dzina lace ndiye Yobu; ndipo munthuyu anali wangwiro ndi woongoka, wakuopa Mulungu ndi kupewa zoipa. 2 Ndipo anabala ana…

Yobu 2

1 Panalinso tsiku lakuti anadza ana a Mulungu kudzionetsa kwa Yehova, nadza Satana yemwe pakati pao kudzionetsa kwa Yehova. 2 Ndipo Yehova anati kwa Satana, Ufuma kuti? Nayankha Satana, nati…

Yobu 3

Madandaulo a Yobu 1 Atatero, Yobu anatsegula pakamwa pace, natemberera tsiku lace. 2 Nalankhula Yobu nati, 3 Litayike tsiku lobadwa ine, Ndi usikuwo udati, Waima naye mwana wamwamuna. 4 Tsiku…

Yobu 4

Elifazi adzudzula Yobu; tsoka la munthu licokera ku zoipa zace; Yobu alape 1 Pamenepo Elifazi wa ku Temani anayankha, nati, 2 Munthu akayesa kunena nawe mau, kodi udzamva nao cisoni?…

Yobu 5

1 Itana tsono; pali wina wakukuyankha kodi? Ndipo udzatembenukira kwa yani wa oyera mtimawo? 2 Pakuti mkwiyo umapha wopusa, Ndi nsanje imakantha wopanda pace. 3 Ndinapenya wopusa woyala mizu; Koma…

Yobu 6

Yobu akuti ali ndi cifukwa ca kudandaula, alira kufa, adzuzula mabwenzi pa kuuma mtima kwao, apempha Mulungu amcitire cifundo 1 Koma Yobu anayankha, nati, 2 Mwenzi atayesa bwino cisoni canga,…

Yobu 7

1 Kodi munthu alibe nkhondo kunja kuno? Kodi masiku ace sakunga masiku a wolembedwa nchito? 2 Monga kapolo woliralira mthunzi, Monga wolembedwa nchito ayembekezera mphotho yace, 3 Momwemo anandilowetsa miyezi…

Yobu 8

Poona tsoka lao Bilidadi akuti Yobu ndi ana ace anacimwa, anena mofanizira 1 Pamenepo anayankha Bilidadi Msuki, nati, 2 Udzanena izi kufikira liti? Ndipo mau a pakamwa pako adzakhala ngati…

Yobu 9

Yobu abvomereza ukulu wa Mulungu, koma okoma ndi oipa alangidwa mmodzimodzi. Masautso ace amfunitsa kufa 1 Pamenepo Yobu anayankha, nati, 2 Zoona, ndidziwa kuti ciri cotero. Koma munthu adzakhala walungama…

Yobu 10

1 Mtima wanga ulema nao moyo wanga, Ndidzadzilolera kudandaula kwanga, Ndidzalankhula pakuwawa mtima wanga. 2 Ndidzati kwa Mulungu, Musanditsutse; Mundidziwitse cifukwa ca kutsutsana nane. 3 Cikukomerani kodi kungosautsa, Kuti mupeputsa…