Yesaya 61

Alalikira Uthenga Wabwino wa cipulumutso 1 Mzimu wa Ambuye Yehova uli pa ine; pakuti Yehova wandidzoza ine ndilalikire mau abwino kwa ofatsa; Iye wanditumiza ndikamange osweka mtima, ndikalalikire kwa am’nsinga…

Yesaya 62

Cikhalidwe cokoma ca Yerusalemu 1 Cifukwa ca Ziyoni sindidzakhala cete, ndi cifukwa ca Yerusalemu sindidzapuma, kufikira cilungamo cace cidzaturuka monga kuyera, ndi cipulumutso cace monga nyali yoyaka. 2 Ndipo amitundu…

Yesaya 63

Mulungu adzapulumutsa anthu ace, nadzabwezera cilango owasautsa 1 Ndani uyu alinkudza kucokera ku Edomu, ndi zobvala zonika zocokera ku Bozira? uyu wolemekezeka m’cobvala cace, nayenda mu ukuru wa mphamvu zace?…

Yesaya 64

1 Mwenzi mutang’amba kumwamba ndi kutsikira pansi, kuti mapiri agwedezeke pamaso panu; 2 monga pamene moto uyatsa zitsamba, ndi moto uwiritsa madzi; kudziwitsa kwa amaliwongo anu dzina lanu, kuti amitundu…

Yesaya 65

Acenjeza osamvera kuti adzalangidwa 1 Iwo amene sanafunsa za Ine andifunafuna; ndi iwo amene sanandipwaira andipeza; ndinati, Taonani Ine, taonani Ine, kwa mtundu umene sunachula dzina langa. 2 Ndatambasulira manja…

Yesaya 66

Ocita zoipa adzabwezedwa cilango 1 Atero Yehova, Kumwamba ndi mpando wanga wacifumu, ndi dziko lapansi ndi coikapo mapazi anga; mudzandimangira Ine nyumba yotani? ndi malo ondiyenera kupumamo ali kuti? 2…