Yesaya 41

Yehova yekha ndiye Mulungu, lsrayeli amkhulupirire Iye yekha yekha 1 Khalani cete pamaso pa Ine, zisumbu inu, anthu atengenso mphamvu; ayandikire; pamenepo alankhule; tiyeni, tiyandikire pamodzi kuciweruziro. 2 Ndani anautsa…

Yesaya 42

Mtumiki wa Yehova 1 Taona Mtumiki wanga, amene ndimgwiriziza; Wosankhika wanga, amene moyo wanga ukondwera naye; ndaika mzimu wanga pa Iye; Iye adzaturutsira amitundu ciweruziro. 2 Iye sadzapfuula, ngakhale kukuwa,…

Yesaya 43

Mulungu Yehova yekha apulumutsa Israyeli 1 Koma tsopano atero Yehova, amene anakulenga iwe Yakobo, ndi Iye amene anakupanga iwe Israyeli, Usaope, cifukwa ndakuombola iwe, ndakuchula dzina lako, iwe uli wanga….

Yesaya 44

Mulungu ndi wamkulukulu, mafano ndi acabe 1 Koma tsopano, imva Yakobo, mtumiki wanga, ndi Israyeli, amene ndakusankha; 2 atero Yehova, amene anakutenga iwe, nakuumba kucokera m’mimba, amene adzathangata iwe. Usaope…

Yesaya 45

Yehova amuyesa Koresi cipangizo cace 1 Atero Yehova kwa wodzozedwa wace kwa Koresi, amene dzanja lace lamanja ndaligwiritsa, kuti agonjetse mitundu ya anthu pamaso pace, ndipo ndidzamasula m’cuuno mwa mafumu;…

Yesaya 46

Aneneratu za kupasuka kwa mafano a ku Babulo 1 Beli agwada pansi, Nebo awerama; mafano ao ali pa zoweta, ndi pa ng’ombe; zinthu zimene inu munanyamula ponseponse ziyesedwa mtolo, katundu…

Yesaya 47

Babulo adzaonongeka konse 1 Tsika, ukhale m’pfumbi, namwaliwe, mwana wamkazi wa Babulo; khala pansi popanda mpando wacifumu, mwana wamkazi wa Akasidi, pakuti iwe sudzayesedwanso wozizira ndi wololopoka. 2 Tenga mipero,…

Yesaya 48

Awadandaulira Aisrayeli, awacenteza, nalonjezana nao 1 Imvani inu ici, banja la Yakobo, amene muchedwa ndi dzina la Israyeli, amene munaturuka m’madzi a Yuda amene mulumbira dzina la Yehova ndi kuchula…

Yesaya 49

Mtumiki wa Yehova, kuunika kwa amitundu 1 Mverani Ine, zisumbu inu, mumvere anthu inu akutari; Yehova anandiitana Ine ndisanabadwe; m’mimba mwa amai Iye anachula dzina langa; 2 nacititsa pakamwa panga…

Yesaya 50

Mtumiki wa Yehova anyozedwa koma athandizidwa 1 Atero Yehova, Kalata wa cilekaniro ca amako ali kuti amene ndinamsudzula naye? pena ndani wa angongole anga amene ndamgulitsa iwe? Taona cifukwa ca…