Yesaya 1
Macimo ndi masauko a ana a lsrayeli 1 MASOMPHENYA a Yesaya mwana wa Amozi, amene iye anaona, onena za Yuda ndi Yerusalemu, masiku a Uziya, Yotamu, Ahazi, ndi Hezekiya, mafumu…
Macimo ndi masauko a ana a lsrayeli 1 MASOMPHENYA a Yesaya mwana wa Amozi, amene iye anaona, onena za Yuda ndi Yerusalemu, masiku a Uziya, Yotamu, Ahazi, ndi Hezekiya, mafumu…
Ulemerero wa Israyeli m’tsogolomo, maweruzo a Mulungu pakatipo 1 Mau amene Yesaya mwana wa Amozi anaona, onena za Yuda ndi Yerusalemu. 2 Ndipo padzakhala masiku otsiriza, kuti phiri la nyumba…
1 Ndipo onani, Ambuye, Yehova wa makamu, wacotsa ku Yerusalemu ndi ku Yuda mcirikizo wocirikiza cakudya conse ndi madzi onse, zimene zinali mcirikizo; 2 munthu wamphamvu, ndi munthu wankhondo; woweruza,…
Tsiku la Mulungu, kuyeretsedwa kwa Yerusalemu 1 Ndipo akazi asanu ndi awiri adzagwira mwamuna mmodzi tsiku limenelo, nati, Ife tidzadya cakudya cathu cathu ndi kubvala zobvala zathu zathu; koma tichedwe…
Fanizo la munda wamphesa ndi kumasulira kwace 1 Ndiyimbire wokondedwa wanga nyimbo ya wokondedwa wanga ya munda wace wamphesa, Wokondedwa wanga anali ndi munda wamphesa m’citunda ca zipatso zambiri; 2…
Masomphenya a Yesaya 1 Caka cimene mfumu Uziya anafa, ndinaona Ambuye atakhala pa mpando wacifumu wautari, ndi wotukulidwa, ndi zobvala zace zinadzala m’Kacisi. 2 Pamwamba pa Iye panaima aserafi; yense…
Rezini ndi Peka akwerera Yerusalemu 1 Ndipo panali masiku a Ahazi, mwana wa Yotamu, mwana wa Uziya, mfumu ya Yuda, kuti Rezini, mfumu ya Aramu, ndi Peka, mwana wa Remaliya,…
Coneneratu cakuti Aasuri adzagonjetsa Israyeli 1 Ndipo Yehova anati kwa ine, Tenga iwe polembapo papakuru, nulembe pamenepo ndi malembedwe odziwika, Kangazakufunkha Fulumirakusakaza, 2 Ndipo ndidzadzitengera ine mboni zokhulupirika, Uriya wansembe,…
Coneneratu ca ufumu wa Mesiya 1 Koma kumene kunali nsautso sikudzakhala kuziya. Poyamba paja Mulungu ananyozetsa dziko la Zebuloni, ndi dziko la Naftali, koma potsiriza pace Iye analicitira ulemu, pa…
1 Tsoka kwa iwo amene alamulira malamulo osalungama, ndi kwa alembi olemba mphulupulu; 2 kuwapatulira osowa kuciweruziro, ndi kucotsera anthu anga aumphawi zoyenera zao, kuti alande za akazi amasiye, nafunkhire…