Yeremiya 51

1 Yehova atero: Taonani, ndidzaukitsira Babulo, ndi iwo okhala m’Lebi-kamai, mphepo yoononga, 2 Ndipo ndidzatuma ku Babulo alendo, amene adzamkupira iye, amene adzataya zonse m’dziko lace, pakuti tsiku la cisauko…

Yeremiya 52

Yerusalemu amangidwa misasa, nalandidwa, napasulidwa 1 Zedekiya anali wa zaka makumi awiri kudza cimodzi pamene analowa ufumu wace; ndipo analamulira m’Yerusalemu zaka khumi kudza cimodzi; dzina la amace ndi Hamutala…