Yeremiya 31

Mwa cikondi ca Mulungu adzabweza Israyeli 1 Nthawi yomweyo, ati Yehova, ndidzakhala Mulungu wa mabanja onse a Israyeli, ndipo iwo adzakhala anthu anga. 2 Atero Yehova, Anthu opulumuka m’lupanga anapeza…

Yeremiya 32

Yeremiya atsekeredwa m’kaidi nagula munda wa Hanameli 1 Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova caka cakhumi ca Zedekiya mfumu ya Yuda, cimene cinali caka cakhumi ndi cisanu ndi…

Yeremiya 33

Yehova abwereza kunena kuti anthu ace adzakhazikikanso m’dziko mwao, padzakhalanso mphukira 1 Ndipo mau a Yehova anadza kwa Yeremiya nthawi yaciwiri, pamene iye anali citsekedwere m’bwalo la kaidi, kuti, 2…

Yeremiya 34

Zedekiya adzatengedwa, Yerusalemu adzalandidwa 1 Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, pamene Nebukadinezara mfumu ya Babulo, ndi nkhondo yace yonse, ndi maufumu onse a dziko lapansi amene anagwira…

Yeremiya 35

Kukhulupirika kwa Arekabu kukhale citsanzo ca kwa Yuda 1 Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova masiku a Yehoyakimu mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, kuti, 2 Pita ku…

Yeremiya 36

Mau a Yeremiya alembedwa pampukutu nawerengedwa m’Kacisi, natenthedwa ndi mfumu 1 Ndipo panali caka cacinai ca Yehoyakimu mwana wa Yosiya, mfumu ya Yuda, mau awa anadza kwa Yeremiya kucokera kwa…

Yeremiya 37

Yeremiya m’kaidi 1 Ndipo Zedekiya mwana wa Yosiya anakhala mfumu m’malo a Koniya mwana wa Yehoyakimu, amene Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo inamlowetsa mfumu m’dziko la Yuda. 2 Koma ngakhale…

Yeremiya 38

Yeremiya aponyedwa m’dzenje muli thope 1 Ndipo Sefatiya mwana wa Matani ndi Gedaliya mwana wa Pusuri, ndi Yukali mwana wa Selemiya, ndi Pasuri mwana wa Malikiya, anamva mau amene Yeremiya…

Yeremiya 39

Nebukadirezara alanda Yerusalemu, nalanditsa Yeremiya 1 Caka cacisanu ndi cinai ca Zedekiya mfumu ya Yuda, mwezi wakhumi, anadza Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo ndi nkhondo yace yonse, ndi kuumangira misasa….

Yeremiya 40

Yeremiya apita kwa Gedaliya ku Mizipa 1 Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, Nebuzaradani kapitao wa alonda atammasula pa Rama, pamene anamtenga iye womangidwa m’maunyolo pamodzi ndi am’nsinga…