Yeremiya 21
Kufunsira kwa Zedekiya, kuyankha kwa Yeremiya 1 Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, pamene Zedekiya mfumu anatuma kwa iye Pasuri mwana wa Malikiya, ndi Zefaniya mwana wace wa…
Kufunsira kwa Zedekiya, kuyankha kwa Yeremiya 1 Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, pamene Zedekiya mfumu anatuma kwa iye Pasuri mwana wa Malikiya, ndi Zefaniya mwana wace wa…
1 Yehova atero: Tsikira ku nyumba ya mfumu ya Yuda, ndi kunena komweko mau awa, 2 ndi kuti, Tamvani mau a Yehova, Inu mfumu ya Yuda, amene mukhala pa mpando…
Mau akutsutsa abusa osakhulupirika 1 Tsoka abusa amene athetsa nabalalitsa nkhosa za busa langa! ati Yehova. 2 Cifukwa cace atero Yehova, Mulungu wa Israyeli, ponenera abusa amene adyetsa anthu anga:…
Za mitanga iwiri ya nkhuyu; za mtundu wao m’tsogolo 1 Yehova anandionetsa ine, ndipo, taonani, mitanga iwiri ya nkhuyu yoikidwa pakhomo pa Kacisi wa Yehova; Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo…
Atalangidwa Aisrayeli adzalangidwa amitundu ena omwe 1 Mau amene anadza kwa Yeremiya za anthu onse a Yuda caka cacinai ca Yehoyakimu mwana wace wa Yosiya, mfumu ya Yuda; ndico caka…
Yeremiya aneneratu za kupasuka kwa Kacisi ndi Yerusalemu. Atsutsidwapo afe 1 Poyamba kukhala mfumu Yehoyakimu mwana wace wa Yosiya, mfumu ya Yuda, panadza mau awa ocokera kwa Yehova, kuti, 2…
Yeremiya awacenjeza agonje kwa mfumu ya ku Babulo 1 Poyamba kukhala mfumu Yehoyakimu mwana wace wa Yosiya, mfumu ya Yuda, mau awa anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, kuti, 2…
Yeremiya atsutsana ndi mneneri wonyenga, Hananiya 1 Ndipo panali caka comweco, poyamba Zedekiya kukhala mfumu ya Yuda, caka cacinai, mwezi wacisanu, kuti Hananiya mwana wa Azuri mneneri, amene anali wa…
Kalata wa Yeremiya wolembera kwa Ayuda otengedwa kunka ku Babulo 1 Amenewa ndi mau a kalata uja anatumiza Yeremiya mneneri kucokera ku Yerusalemu kunka kwa akuru otsala a m’nsinga, ndi…
Yehova alonjeza kubweza undende wa anthu a Israyeli 1 Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, kuti, 2 Atero Yehova, Mulungu wa Israyeli, kuti, Lemba m’buku mau onse amene…