Yeremiya 11

Za kutyola panganolo 1 Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, kuti, 2 Imvani mau a pangano ili, nenani kwa anthu a Yuda, ndi anthu a Yerusalemu; 3 ndi…

Yeremiya 12

1 Wolungama ndinu, Yehova, pamene nditsutsana nanu mlandu; pokhapo ndinenane nanu za maweruzo; cifukwa canji ipindula njira ya oipa? cifukwa canji akhala bwino onyengetsa? 2 Inu mwabzyala iwo, inde, anagwiritsatu…

Yeremiya 13

Fanizo la mpango wabafuta lifanizira kulangidwa kwao 1 Atero Yehova kwa ine, Pita, udzigulire mpango wabafuta, nudzimangire m’cuuno mwako, usauike m’madzi. 2 Ndipo ndinagula mpango monga mwa mau a Yehova,…

Yeremiya 14

Yeremiya apempherera anthu 1 Mau a Yehova amene anadza kwa Yeremiya onena za cirala. 2 Yuda alira, ndipo zipata zace zilefuka, zikhala pansi zobvekedwa ndi zakuda; mpfuu wa Yerusalemu wakwera….

Yeremiya 15

Yehova akanadi kumvera 1 Ndipo Yehova anati kwa ine, Ngakhale Mose ndi Samueli akadaima pamaso panga, koma mtima wanga sukadasamalira anthu awa; muwacotse iwo pamaso panga, aturuke. 2 Ndipo padzakhala,…

Yeremiya 16

Aneneratu za kutengedwa ukapolo kwa Israyeli ndi kubweranso kwao 1 Ndiponso mau a Mulungu anadza kwa ine, kuti, 2 Usatenge mkazi, usakhale ndi ana amuna ndi akazi m’malo muno. 3…

Yeremiya 17

Cimo la Yuda ndi losafafanizika 1 Cimo la Yuda lalembedwa ndi peni lacitsulo, ndi nsonga ya diamondi; lalembedwa pa colembapo ca m’mtima mwao, ndi pa nyanga za maguwa a nsembe…

Yeremiya 18

Mbiya ya woumba. Anthu osalapa 1 Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, kuti, 2 Tauka, tatsikira ku nyumba ya woumba, pamenepo ndidzakumvetsa mau anga. 3 Ndipo ndinatsikira ku…

Yeremiya 19

Nsupa ya woumba isweka, Yerusalemu apasuka 1 Atero Yehova, Pita, nugule nsupa ya woumba, nutenge akuru a anthu, ndi akuru a ansembe; 2 nuturukire ku cigwa ca mwana wace wa…

Yeremiya 20

Pasuri wansembe apanda Yeremiya, nammanga m’kaidi 1 Ndipo Pasuri mwana wace wa Imeri wansembe, amene anali kapitao wamkuru m’nyumba ya Yehova, anamva Yeremiya alikunenera zimenezi. 2 Ndipo Pasuri anampanda Yeremiya…