Yeremiya 1
Kuitanidwa kwa Yeremiya akhale mneneri 1 MAU a Yeremiya mwana wa Hilikiya, wa ansembe amene anali ku Anatoti m’dziko la Benjamini; 2 amene anamdzera mau a Yehova masiku a Yosiya…
Kuitanidwa kwa Yeremiya akhale mneneri 1 MAU a Yeremiya mwana wa Hilikiya, wa ansembe amene anali ku Anatoti m’dziko la Benjamini; 2 amene anamdzera mau a Yehova masiku a Yosiya…
Yehova adzudzula anthu a lsrayeli 1 Ndipo mau a Yehova anadza kwa ine, nati, 2 Pita nupfuule n’makutu a Yerusalemu, kuti, Yehova atero, Ndikumbukira za iwe kukoma mtima kwa ubwana…
1 Amati, Ngati mwamuna acotsa mkazi wace, ndipo amcokera iye, nakhala mkazi wa wina, kodi adzabweranso kwa mkaziyo? dzikolo kodi silidzaipitsidwa? Koma iwe wacita dama ndi mabwenzi ambiri; koma bweranso…
1 Ngati udzabwera, Israyeli, ati Yehova, udzabwera kwa Ine; ndipo ngati udzacotsa zonyansa zako pamaso panga sudzacotsedwa. 2 Ndipo udzalumbira, Pali Yehova m’zoonadi, m’ciweruziro, ndi m’cilungamo; ndipo mitundu ya anthu…
Malango a Mulungu pa Ayuda cifukwa ca zoipa zao zonse 1 Thamangani inu kwina ndi kwina m’miseu ya Yerusalemu, taonanitu, dziwani, ndi kufunafuna m’mabwalo ace, kapena mukapeza munthu, kapena alipo…
Acenjezedwa kuti adani adzamangira Yerusalemu misasa 1 Ananu a Benjamini, pulumukani pothawa pakati pa Yerusalemu, ombani lipenga m’Tekoa, kwezani cizindikiro m’Beti-hakeremu; pakuti caoneka coipa coturuka m’mpoto ndi kuononga kwakukulu. 2…
Mneneri alikuima pa cipata ca Kacisi, achula mau akulonieza ndi akuopsa 1 Mau amene anadza kwa Yeremiya kucokera kwa Yehova, kuti, 2 Ima m’cipata ca nyumba ya Yehova, lalikira m’menemo…
1 Nthawi yomweyo, ati Yehova, adzaturutsa m’manda mwao mafupa a mafumu a Yuda, ndi mafupa a akuru ace, ndi mafupa a ansembe, ndi mafupa a aneneri, ndi mafupa a okhala…
1 Ha, mutu wanga ukadakhala madzi, ndi maso anga kasupe wa misozi, kuti usana ndi usiku ndilirire ophedwa a mwana wamkazi wa anthu anga! 2 Ha, ndikadakhala ndi cigono ca…
Mofano ndi acabe, Yehova ndiye 1 Tamvani mau amene Yehova anena kwa inu, nyumba ya Israyeli; 2 atero Yehova, a Musaphunzire njira ya amitundu, musaope zizindikiro za m’thambo; pakuti amitundu…